Ndandanda ya Mlungu wa March 23
MLUNGU WOYAMBIRA MARCH 23
Nyimbo Na. 73 ndi Pemphero
Phunziro la Baibulo la Mpingo:
cl mutu 10 ndime 8-17 (Mph. 30)
Sukulu ya Utumiki wa Mulungu:
Kuwerenga Baibulo: 1 Samueli 10-13 (Mph. 8)
Na. 1: 1 Samueli 11:1-10 (Osapitirira mph. 3)
Na. 2: Kodi Baibulo Linaneneratu Zinthu Ziti Zokhudza Masiku Ano?—igw tsa. 12 ndime 1-4 (Mph. 5)
Na. 3: Tingatani Kuti Tikhale Ndi Chikhulupiriro Kuyambira Tili Ana Mpaka Kukula?—yp2 tsa. 290-293 (Mph. 5)
Msonkhano wa Utumiki:
Mutu wa Mwezi Uno: ‘Khalani Okonzekera Ntchito Iliyonse Yabwino.’—Tito 3:1.
Mph. 30: “Mungatani Kuti Msonkhano Wokonzekera Utumiki Uzikhala Wothandiza?” Mafunso ndi mayankho.
Nyimbo Na. 32 ndi Pemphero