Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • mwb16 November tsamba 4
  • November 14-20

Palibe Vidiyo.

Pepani vidiyoyi ikukanika kutsegula.

  • November 14-20
  • Utumiki Komanso Moyo Wathu wa Chikhristu—Ndandanda ya Misonkhano—2016
Utumiki Komanso Moyo Wathu wa Chikhristu—Ndandanda ya Misonkhano—2016
mwb16 November tsamba 4

November 14-20

MLALIKI 1-6

  • Nyimbo Na. 66 ndi Pemphero

  • Mawu Oyamba (Osapitirira 3 min.)

CHUMA CHOPEZEKA M’MAWU A MULUNGU

  • “Muzisangalala Chifukwa Chogwira Ntchito Mwakhama”: (10 min.)

    • [Onetsani vidiyo yakuti, Mfundo Zothandiza Kumvetsa Buku la Mlaliki.]

    • Mlal. 3:12, 13—Kusangalala ndi ntchito ndi mphatso yochokera kwa Mulungu (w15 2/1 4–6)

    • Mlal. 4:6—Tiziona moyenera ntchito yathu (w15 2/1 6 ndime 3-5)

  • Kufufuza Mfundo Zothandiza: (8 min.)

    • Mlal. 2:10, 11—Kodi Solomo anazindikira mfundo iti yokhudza chuma? (w08 4/15 22 ndime 9-10)

    • Mlal. 3:16, 17—Kodi tiyenera kuona bwanji zinthu zopanda chilungamo zimene zimachitika m’dzikoli? (w06 11/1 14 ndime 8)

    • Kodi ndaphunzira zotani zokhudza Yehova pa kuwerenga Baibulo kwa mlungu uno?

    • Kodi ndi mfundo ziti zimene ndaphunzira pa kuwerenga Baibulo kwa mlungu uno zimene ndingazigwiritse ntchito mu utumiki?

  • Kuwerenga Baibulo: (Osapitirira 4 min.) Mlal. 1:1-18

KUPHUNZITSA MWALUSO MU UTUMIKI

  • Ulendo Woyamba: (Osapitirira 2 min.) Nkhani yokhudza mutu wa pachikuto wa wp16.6—M’patseni munthuyo khadi lodziwitsa anthu za JW.ORG.

  • Ulendo Wobwereza: (Osapitirira 4 min.) Nkhani yokhudza mutu wa pachikuto wa wp16.6—Werengani malemba pogwiritsa ntchito foni kapena tabuleti.

  • Phunziro la Baibulo: (Osapitirira 6 min.) bhs 22-23 ndime 11-12—Muitanireni munthuyo kumisonkhano.

MOYO WATHU WACHIKHRISTU

  • Nyimbo Na. 140

  • “Kodi Tingagwiritse Ntchito Bwanji Buku Lakuti Zimene Baibulo Limaphunzitsa?”: (15 min.) Nkhani yokambirana. Kenako, onetsani ndiponso kukambirana vidiyo yosonyeza mbali yochepa ya phunziro la Baibulo pogwiritsa ntchito mfundo na. 4 patsamba 115 m’buku lakuti Zimene Baibulo Limaphunzitsa.

  • Phunziro la Baibulo la Mpingo: (30 min.) ia mutu 11 ndime 1-11

  • Mfundo Zimene Taphunzira Komanso za Mlungu Wamawa (3 min.)

  • Nyimbo Na. 112 ndi Pemphero

    Mabuku a Chichewa (1974-2025)
    Tulukani
    Lowani
    • Chichewa
    • Tumizirani Ena
    • Zimene Mumakonda
    • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
    • Zoyenera Kutsatira
    • Nkhani Yosunga Chinsinsi
    • Privacy Settings
    • JW.ORG
    • Lowani
    Tumizirani Ena