Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • mwb16 December tsamba 2
  • December 5-11

Palibe Vidiyo.

Pepani vidiyoyi ikukanika kutsegula.

  • December 5-11
  • Utumiki Komanso Moyo Wathu wa Chikhristu—Ndandanda ya Misonkhano—2016
Utumiki Komanso Moyo Wathu wa Chikhristu—Ndandanda ya Misonkhano—2016
mwb16 December tsamba 2

December 5-11

YESAYA 1-5

  • Nyimbo Na. 107 ndi Pemphero

  • Mawu Oyamba (Osapitirira 3 min.)

CHUMA CHOPEZEKA M’MAWU A MULUNGU

  • “Tiyeni Tipite Kukakwera Phiri la Yehova”: (10 min.)

    • [Onetsani vidiyo yakuti, Mfundo Zothandiza Kumvetsa Buku la Yesaya.]

    • Yes. 2:2, 3—“Phiri la nyumba ya Yehova” limaimira kulambira koyera (ip-1 38-41 ¶6-11; 45 ¶20-21)

    • Yes. 2:4—Anthu olambira Yehova samenya nkhondo (ip-1 46-47 ¶24-25)

  • Kufufuza Mfundo Zothandiza: (8 min.)

    • Yes. 1:8, 9—Kodi mawu oti “Mwana wamkazi wa Ziyoni wasiyidwa ngati msasa m’munda wa mpesa” akutanthauza chiyani? (w06 12/1 8 ¶5)

    • Yes. 1:18—Kodi Yehova ankatanthauza chiyani pouza Aisiraeli kuti “tiyeni tikambirane”? (w06 12/1 9 ¶1; it-2-E 761 ¶3)

    • Kodi ndaphunzira zotani zokhudza Yehova pa kuwerenga Baibulo kwa mlungu uno?

    • Kodi ndi mfundo ziti zimene ndaphunzira pa kuwerenga Baibulo kwa mlungu uno zimene ndingazigwiritse ntchito mu utumiki?

  • Kuwerenga Baibulo: (Osapitirira 4 min.) Yes. 5:1-13

KUPHUNZITSA MWALUSO MU UTUMIKI

  • Kukonzekera Ulaliki wa Mwezi Uno: (15 min.) Nkhani yokambirana pogwiritsa ntchito “Zitsanzo za Ulaliki.” Pambuyo poonetsa vidiyo iliyonse ya chitsanzo cha ulaliki, kambiranani mfundo zimene tikuphunzirapo. Limbikitsani ofalitsa kuti azilemba ulaliki wawowawo.

MOYO WATHU WACHIKHRISTU

  • Nyimbo Na. 139

  • Zofunika Pampingo: (7 min.) Mukhoza kukambirana mfundo zimene tikuphunzira mu Buku Lapachaka. (yb16 32 ¶3–34 ¶1)

  • “Kuwonjezera Luso Lathu mu Utumiki—Tizifika Anthu Pamtima ndi Buku Lakuti Kodi Mungatani Kuti ‘Mulungu Apitirize Kukukondani’?”: (8 min.) Nkhani yokambirana. Limbikitsani onse amene ali ndi mbali ya Phunziro la Baibulo mwezi uno kuti agwiritse ntchito mfundo zopezeka patsamba 261-262 m’buku la Sukulu ya Utumiki.

  • Phunziro la Baibulo la Mpingo: (30 min.) ia mutu 12 ¶13-25 komanso Mfundo Zofunika Kuziganizira patsamba 107.

  • Mfundo Zimene Taphunzira Komanso za Mlungu Wamawa (3 min.)

  • Nyimbo Na. 154 ndi Pemphero

    Kumbukirani: Muyenera kuika nyimboyi kuti onse amvetsere, kenako muibwerezenso kuti onse aimbe nawo.

    Mabuku a Chichewa (1974-2025)
    Tulukani
    Lowani
    • Chichewa
    • Tumizirani Ena
    • Zimene Mumakonda
    • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
    • Zoyenera Kutsatira
    • Nkhani Yosunga Chinsinsi
    • Privacy Settings
    • JW.ORG
    • Lowani
    Tumizirani Ena