Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • mwb17 March tsamba 6
  • March 27–April 2

Palibe Vidiyo.

Pepani vidiyoyi ikukanika kutsegula.

  • March 27–April 2
  • Utumiki Komanso Moyo Wathu wa Chikhristu—Ndandanda ya Misonkhano—2017
Utumiki Komanso Moyo Wathu wa Chikhristu—Ndandanda ya Misonkhano—2017
mwb17 March tsamba 6

March 27–April 2

YEREMIYA 12-16

  • Nyimbo Na. 135 ndi Pemphero

  • Mawu Oyamba (Osapitirira 3 min.)

CHUMA CHOPEZEKA M’MAWU A MULUNGU

  • “Aisiraeli Anaiwala Yehova”: (10 min.)

    • Yer. 13:1-5​—Yeremiya anamvera malangizo a Mulungu oti akabise lamba ngakhale kuti zinali zovuta (jr 51 ¶17)

    • Yer. 13:6, 7​—Yeremiya atayenda ulendo wautali kuti akatenge lamba uja, anapeza kuti anali atawonongeka (jr 52 ¶18)

    • Yer. 13:8-11​—Yehova anasonyeza kuti ubwenzi wolimba umene anali nawo ndi Aisiraeli udzawonongeka, kapena kuti kusokonekera, chifukwa chakuti iwo anali anthu osamva (jr 52 ¶19-20; it-1-E 1121 ¶2)

  • Kufufuza Mfundo Zothandiza: (8 min.)

    • Yer. 12:1, 2, 14​—Kodi Yeremiya anafunsa funso lotani ndipo Yehova anamuyankha bwanji? (jr 118 ¶11)

    • Yer. 15:17​—Kodi Yeremiya ankaona bwanji nkhani yosankha anthu ocheza nawo, nanga tingamutsanzire bwanji? (w04 5/1 11 ¶16)

    • Kodi ndaphunzira zotani zokhudza Yehova pa kuwerenga Baibulo kwa mlungu uno?

    • Kodi ndi mfundo ziti zimene ndaphunzira pa kuwerenga Baibulo kwa mlungu uno zimene ndingazigwiritse ntchito mu utumiki?

  • Kuwerenga Baibulo: (Osapitirira 4 min.) Yer. 13:15-27

KUPHUNZITSA MWALUSO MU UTUMIKI

  • Ulendo Woyamba: (Osapitirira 2 min.) Kapepala koitanira anthu ku Chikumbutso komanso vidiyo—Muuzeni zimene mudzakambirane ulendo wotsatira.

  • Ulendo Wobwereza: (Osapitirira 4 min.) Kapepala koitanira anthu ku Chikumbutso komanso video​—Muuzeni zimene mudzakambirane ulendo wotsatira.

  • Nkhani: (6 min.) w16.03 29-31​—Mutu: Kodi Anthu a Mulungu Analowa Liti mu Ukapolo wa M’Babulo Wamkulu?

MOYO WATHU WACHIKHRISTU

  • Nyimbo Na. 139

  • “Muzithandiza Banja Lanu Kuti Lizikumbukira Yehova” (15 min.) Nkhani Yokambirana. Yambani ndi kuonetsa vidiyo yakuti “Mawu Awa . . . Azikhala Pamtima Pako”—Kucheza ndi Mabanja.

  • Phunziro la Baibulo la Mpingo: (30 min.) ia mutu 20 ¶14-26 komanso Mfundo Zofunika Kuziganizira patsamba 179

  • Mfundo Zimene Taphunzira Komanso za Mlungu Wamawa (3 min.)

  • Nyimbo Na. 48 ndi Pemphero

    Mabuku a Chichewa (1974-2025)
    Tulukani
    Lowani
    • Chichewa
    • Tumizirani Ena
    • Zimene Mumakonda
    • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
    • Zoyenera Kutsatira
    • Nkhani Yosunga Chinsinsi
    • Privacy Settings
    • JW.ORG
    • Lowani
    Tumizirani Ena