Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • mwb17 May tsamba 7
  • May 29-June 4

Palibe Vidiyo.

Pepani vidiyoyi ikukanika kutsegula.

  • May 29-June 4
  • Utumiki Komanso Moyo Wathu wa Chikhristu—Ndandanda ya Misonkhano—2017
Utumiki Komanso Moyo Wathu wa Chikhristu—Ndandanda ya Misonkhano—2017
mwb17 May tsamba 7

May 29–June 4

YEREMIYA 49-50

  • Nyimbo Na. 102 ndi Pemphero

  • Mawu Oyamba (Osapitirira 3 min.)

CHUMA CHOPEZEKA M’MAWU A MULUNGU

  • “Yehova Amadalitsa Anthu Odzichepetsa Ndipo Amalanga Odzikuza”: (10 min.)

    • Yer. 50:4-7​—Aisiraeli odzichepetsa omwe analapa anamasulidwa ku ukapolo ndipo anabwerera ku Ziyoni

    • Yer. 50:29-32​—Babulo anawonongedwa chifukwa chochita zinthu modzikuza (it-1 54)

    • Yer. 50:38, 39​—M’Babulo simudzakhalanso anthu (jr 161 ¶15; w98 4/1 20 ¶20)

  • Kufufuza Mfundo Zothandiza: (8 min.)

    • Yer. 49:1, 2​—N’chifukwa chiyani Yehova anadzudzula a Amoni? (it-1-E 94 ¶6)

    • Yer. 49:17, 18​—Kodi Edomu anafanana bwanji ndi Sodomu ndi Gomora, ndipo n’chifukwa chiyani? (jr 163 ¶18; ip-2 351 ¶6)

    • Kodi mwaphunzira zotani zokhudza Yehova pa kuwerenga Baibulo kwa mlungu uno?

    • Kodi ndi mfundo zina ziti zothandiza zimene mwapeza pa kuwerenga Baibulo kwa mlungu uno?

  • Kuwerenga Baibulo: (Osapitirira 4 min.) Yer. 50:1-10

KUPHUNZITSA MWALUSO MU UTUMIKI

  • Ulendo Woyamba: (Osapitirira 2 min.) T-32​—Muuzeni zimene mudzakambirane ulendo wotsatira.

  • Ulendo Wobwereza: (Osapitirira 4 min.) T-32​—Kambiranani kachigawo kakuti “Ganizirani Mfundo Iyi.” Muuzeni zimene mudzakambirane ulendo wotsatira.

  • Nkhani: (Osapitirira 6 min.) w15 3/15 17-18​—Mutu: N’chifukwa Chiyani Masiku Ano Mabuku Athu Safotokoza Kwambiri Kuti Zinthu Zosiyanasiyana Zotchulidwa m’Baibulo Zimaphiphiritsira Zinazake?

MOYO WATHU WACHIKHRISTU

  • Nyimbo Na. 64

  • Chotsa Mtanda wa Denga M’diso Lako: (15 min.) Onetsani vidiyo yakuti Chotsa Mtanda wa Denga M’diso Lako. Kenako kambiranani mafunso otsatirawa: Kodi m’bale wina wasonyeza bwanji kuti anali wonyada komanso wokonda kuweruza ena? N’chiyani chamuthandiza kuti asinthe maganizo? Nanga kodi wapindula bwanji?

  • Phunziro la Baibulo la Mpingo: (30 min.) kr mutu 1 ¶11-20

  • Mfundo Zimene Taphunzira Komanso za Mlungu Wamawa (3 min.)

  • Nyimbo Na. 131 ndi Pemphero

    Mabuku a Chichewa (1974-2025)
    Tulukani
    Lowani
    • Chichewa
    • Tumizirani Ena
    • Zimene Mumakonda
    • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
    • Zoyenera Kutsatira
    • Nkhani Yosunga Chinsinsi
    • Privacy Settings
    • JW.ORG
    • Lowani
    Tumizirani Ena