May Utumiki komanso Moyo Wathu Wachikhristu—Ndandanda ya May 2017 Zitsanzo za Ulaliki May 1-7 CHUMA CHOPEZEKA M’MAWU A MULUNGU | YEREMIYA 32-34 Chizindikiro Chosonyeza Kuti Aisiraeli Adzabwerera Kwawo May 8-14 CHUMA CHOPEZEKA M’MAWU A MULUNGU | YEREMIYA 35-38 Ebedi-meleki Ndi Chitsanzo Chabwino pa Nkhani ya Kulimba Mtima Komanso Kukoma Mtima MOYO WATHU WACHIKHRISTU Kusamalira Malo Athu Olambirira May 15-21 CHUMA CHOPEZEKA M’MAWU A MULUNGU | YEREMIYA 39-43 Yehova Adzaweruza Aliyense Malinga ndi Ntchito Zake MOYO WATHU WACHIKHRISTU Yehova Sangaiwale Chikondi Chanu May 22-28 CHUMA CHOPEZEKA M’MAWU A MULUNGU | YEREMIYA 44-48 Leka ‘Kufunafuna Zinthu Zazikulu’ May 29-June 4 CHUMA CHOPEZEKA M’MAWU A MULUNGU | YEREMIYA 49-50 Yehova Amadalitsa Anthu Odzichepetsa Ndipo Amalanga Odzikuza