December 25-31
MALAKI 1-4
Nyimbo Na. 36 ndi Pemphero
Mawu Oyamba (Osapitirira 3 min.)
CHUMA CHOPEZEKA M’MAWU A MULUNGU
“Kodi Ukwati Wanu Umakondweretsa Yehova?”: (10 min.)
[Onetsani vidiyo yakuti Mfundo Zothandiza Kumvetsa Buku la Malaki.]
Mal. 2:13, 14—Yehova amadana ndi khalidwe lachinyengo m’banja (jd 125-126 ¶4-5)
Mal. 2:15, 16—Muzikhala wokhulupirika kwa mwamuna kapena mkazi wanu (w02 5/1 18 ¶19)
Kufufuza Mfundo Zothandiza: (8 min.)
Mal. 1:10—N’chifukwa chiyani tiyenera kuchita zinthu zokhudza kulambira chifukwa chokonda Mulungu komanso anzathu? (w07 12/15 27 ¶1)
Mal. 3:1—Kodi vesili linakwaniritsidwa bwanji m’nthawi ya atumwi komanso m’nthawi yathu ino? (w13 7/15 10-11 ¶5-6)
Kodi mwaphunzira zotani zokhudza Yehova pa kuwerenga Baibulo kwa mlungu uno?
Kodi ndi mfundo zina ziti zothandiza zimene mwapeza pa kuwerenga Baibulo kwa mlungu uno?
Kuwerenga Baibulo: (Osapitirira 4 min.) Mal. 1:1-10
KUPHUNZITSA MWALUSO MU UTUMIKI
Ulendo Woyamba: (Osapitirira 2 min.) 1 Akor. 15:26—Kuphunzitsa Choonadi.
Ulendo Wobwereza: (Osapitirira 4 min.) Yes. 26:19; 2 Akor. 1:3, 4—Kuphunzitsa Choonadi. (Onani mwb16.08 8 ¶2.)
Nkhani: (Osapitirira 6 min.) w07 12/15 28 ¶1—Mutu: Kodi Masiku Ano Timapereka Bwanji kwa Yehova Gawo Limodzi mwa Magawo 10 Alionse a Zinthu Zathu?
MOYO WATHU WACHIKHRISTU
“Chikondi Chenicheni”: (15 min.) Mafunso ndi mayankho.
Phunziro la Baibulo la Mpingo: (30 min.) kr mutu 12 ¶1-8 komanso tsamba 121
Mfundo Zimene Taphunzira Komanso za Mlungu Wamawa (3 min.)
Nyimbo Na. 114 ndi Pemphero