Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • mwb18 August tsamba 2
  • August 6-12

Palibe Vidiyo.

Pepani vidiyoyi ikukanika kutsegula.

  • August 6-12
  • Utumiki Komanso Moyo Wathu wa Chikhristu—Ndandanda ya Misonkhano—2018
Utumiki Komanso Moyo Wathu wa Chikhristu—Ndandanda ya Misonkhano—2018
mwb18 August tsamba 2

August 6-12

Luka 17-18

  • Nyimbo Na. 18 ndi Pemphero

  • Mawu Oyamba (Osapitirira 3 min.)

CHUMA CHOPEZEKA M’MAWU A MULUNGU

  • “Muzisonyeza Kuyamikira”: (10 min.)

    • Luka 17:11-14​—Yesu anachiritsa anthu 10 akhate (“amuna 10 akhate” “Pitani mukadzionetse kwa ansembe” mfundo zimene ndikuphunzira pa Luka 17:12, 14, nwtsty)

    • Luka 17:15, 16​—Munthu mmodzi yekha ndi amene anabwerera kukathokoza kwa Yesu

    • Luka 17:17, 18​—Nkhani imeneyi ikutithandiza kuona kufunika kosonyeza kuyamikira (w08 8/1 14-15 ¶9-10)

  • Kufufuza Mfundo Zothandiza: (8 min.)

    • Luka 17:7-10​—Kodi mfundo yaikulu mu fanizo la Yesu palembali ndi yotani? (“opanda pake” mfundo zimene ndikuphunzira pa Luka 17:10, nwtsty)

    • Luka 18:8​—Kodi ndi chikhulupiriro chotani chimene Yesu ankanena palembali? (“chikhulupiriro” mfundo zimene ndikuphunzira pa Luka 18:8, nwtsty)

    • Kodi mwaphunzira zotani zokhudza Yehova pa kuwerenga Baibulo kwa mlungu uno?

    • Kodi ndi mfundo zina ziti zothandiza zimene mwapeza pa kuwerenga Baibulo kwa mlungu uno?

  • Kuwerenga Baibulo: (Osapitirira 4 min.) Luka 18:24-43

KUPHUNZITSA MWALUSO MU UTUMIKI

  • Vidiyo ya Ulendo Woyamba: (4 min.) Onerani ndi kukambirana mfundo za m’vidiyoyi.

  • Ulendo Wobwereza Woyamba: (Osapitirira 3 min.) Gwiritsani ntchito chitsanzo cha zimene tinganene.

  • Phunziro la Baibulo: (Osapitirira 6 min.) fg phunziro 4 ¶1-2

MOYO WATHU WACHIKHRISTU

  • Nyimbo Na. 39

  • “Kumbukirani Mkazi wa Loti”: (15 min.) Nkhani yokambirana.

  • Phunziro la Baibulo la Mpingo: (30 min.) kr mutu 22 ¶17-24 komanso bokosi patsamba 240

  • Mfundo Zimene Taphunzira Komanso za Mlungu Wamawa (3 min.)

  • Nyimbo Na. 117 ndi Pemphero

    Mabuku a Chichewa (1974-2025)
    Tulukani
    Lowani
    • Chichewa
    • Tumizirani Ena
    • Zimene Mumakonda
    • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
    • Zoyenera Kutsatira
    • Nkhani Yosunga Chinsinsi
    • Privacy Settings
    • JW.ORG
    • Lowani
    Tumizirani Ena