Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • mwb18 August tsamba 2
  • Muzisonyeza Kuyamikira

Palibe Vidiyo.

Pepani vidiyoyi ikukanika kutsegula.

  • Muzisonyeza Kuyamikira
  • Utumiki Komanso Moyo Wathu wa Chikhristu—Ndandanda ya Misonkhano—2018
  • Nkhani Yofanana
  • N’chifukwa Chiyani Tiyenera Kusonyeza Kuti Timayamikira?
    Nsanja ya Olonda—2008
  • Kodi Mudzachita Zinthu Zosonyeza Kuyamikira Yehova pa Nyengo ya Chikumbutso Ikubwerayi?
    Utumiki Wathu wa Ufumu—2014
  • Muziphunzitsa Ana Anu Kukhala ndi Mtima Woyamikira
    Mfundo Zothandiza Mabanja
  • ‘Kodi Yehova Ndidzamubwezera Chiyani?’
    Utumiki Komanso Moyo Wathu wa Chikhristu—Ndandanda ya Misonkhano—2016
Onani Zambiri
Utumiki Komanso Moyo Wathu wa Chikhristu—Ndandanda ya Misonkhano—2018
mwb18 August tsamba 2

CHUMA CHOPEZEKA M’MAWU A MULUNGU | LUKA 17-18

Muzisonyeza Kuyamikira

17:11-18

Akhate 10 anabwera kwa Yesu kudzapempha kuti awachiritse, koma atachiritsidwa, ndi mmodzi yekha amene anabwerera kudzathokoza

Kodi nkhani imeneyi ikutiphunzitsa chiyani pa nkhani yosonyeza kuyamikira?

  • Tisamangothokoza chamumtima koma tizichita zinthu zosonyeza kuti tikuyamikira

  • Munthu akamayamikira kuchokera pansi pa mtima amasonyeza kuti ali ndi makhalidwe abwino komanso amakonda Akhristu anzake

  • Anthu amene amafuna kusangalatsa Khristu amayesetsa kukonda komanso kuyamikira anthu onse, mosasamala kanthu kuti ndi osiyana nawo mtundu kapena chipembedzo

Kodi ndi liti pamene ndinayamikira munthu wina chifukwa chondithandiza?

Kodi ndi liti pamene ndinalemba kalata yosonyeza kuthokoza pa zimene wina anandichitira?

Mlongo akulemba kalata yothokoza
    Mabuku a Chichewa (1974-2025)
    Tulukani
    Lowani
    • Chichewa
    • Tumizirani Ena
    • Zimene Mumakonda
    • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
    • Zoyenera Kutsatira
    • Nkhani Yosunga Chinsinsi
    • Privacy Settings
    • JW.ORG
    • Lowani
    Tumizirani Ena