Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • mwb19 February tsamba 5
  • February 18-24

Palibe Vidiyo.

Pepani vidiyoyi ikukanika kutsegula.

  • February 18-24
  • Utumiki Komanso Moyo Wathu wa Chikhristu—Ndandanda ya Misonkhano—2019
Utumiki Komanso Moyo Wathu wa Chikhristu—Ndandanda ya Misonkhano—2019
mwb19 February tsamba 5

February 18-24

AROMA 7-8

  • Nyimbo Na. 27 ndi Pemphero

  • Mawu Oyamba (Osapitirira 3 min.)

CHUMA CHOPEZEKA M’MAWU A MULUNGU

  • “Kodi ‘Mukudikira Mwachidwi’?”: (10 min.)

    • Aroma 8:19​—“Ulemerero wa ana a Mulungu” uonekera posachedwapa (w12 7/15 11 ¶17)

    • Aroma 8:20​—“Chilengedwe chinaperekedwa ku mkhalidwe wopanda pake . . . pa maziko a chiyembekezo” (w12 3/15 23 ¶11)

    • Aroma 8:21​—Chilengedwe “chidzamasulidwa ku ukapolo wa kuvunda” (w12 3/15 23 ¶12)

  • Kufufuza Mfundo Zothandiza: (8 min.)

    • Aroma 8:6​—Kodi “kuika maganizo pa zinthu za thupi,” kumasiyana bwanji ndi “kuika maganizo pa zinthu za mzimu”? (w17.06 3)

    • Aroma 8:26, 27​—Kodi Yehova amayankha bwanji “madandaulo amene sitinathe kuwafotokoza”? (w09 11/15 7 ¶20)

    • Kodi mwaphunzira zotani zokhudza Yehova pa kuwerenga Baibulo kwa mlungu uno?

    • Kodi ndi mfundo zina ziti zothandiza zimene mwapeza pa kuwerenga Baibulo kwa mlungu uno?

  • Kuwerenga Baibulo: (Osapitirira 4 min.) Aroma 7:13-25 (th phunziro 10)

KUPHUNZITSA MWALUSO MU UTUMIKI

  • Vidiyo ya Ulendo Wobwereza Woyamba: (5 min.) Onerani ndi kukambirana mfundo za m’vidiyoyi.

  • Ulendo Wobwereza Woyamba: (Osapitirira 3 min.) Gwiritsani ntchito chitsanzo cha ulendo wobwereza woyamba. (th phunziro 6)

  • Ulendo Wobwereza Woyamba: (Osapitirira 5 min.) Yambani ndi chitsanzo cha ulendo wobwereza woyamba. Musonyezeni ndi kukambirana mfundo za m’vidiyo yakuti Kodi Phunziro la Baibulo Limachitika Bwanji? (koma musaonetse vidiyoyi). (th phunziro 9)

MOYO WATHU WACHIKHRISTU

  • Nyimbo Na. 139

  • “Pitirizani Kudikira Mopirira”: (15 min.) Nkhani yokambirana. Onerani vidiyo yakuti Tiyenera ‘Kuthamanga Mopirira’​—Musamakayikire Kuti Mudzapeza Mphoto.

  • Phunziro la Baibulo la Mpingo: (30 min.) jy mutu 26

  • Mfundo Zimene Taphunzira Komanso za Mlungu Wamawa (3 min.)

  • Nyimbo Na. 105 ndi Pemphero

    Mabuku a Chichewa (1974-2025)
    Tulukani
    Lowani
    • Chichewa
    • Tumizirani Ena
    • Zimene Mumakonda
    • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
    • Zoyenera Kutsatira
    • Nkhani Yosunga Chinsinsi
    • Privacy Settings
    • JW.ORG
    • Lowani
    Tumizirani Ena