Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • mwb19 February tsamba 6
  • February 25–March 3

Palibe Vidiyo.

Pepani vidiyoyi ikukanika kutsegula.

  • February 25–March 3
  • Utumiki Komanso Moyo Wathu wa Chikhristu—Ndandanda ya Misonkhano—2019
Utumiki Komanso Moyo Wathu wa Chikhristu—Ndandanda ya Misonkhano—2019
mwb19 February tsamba 6

February 25–March 3

AROMA 9-11

  • Nyimbo Na. 25 ndi Pemphero

  • Mawu Oyamba (Osapitirira 3 min.)

CHUMA CHOPEZEKA M’MAWU A MULUNGU

  • “Fanizo la Mtengo wa Maolivi”: (10 min.)

    • Aroma 11:16​—Mtengo wa Maolivi umaimira kukwaniritsidwa kwa cholinga cha Mulungu chokhudza pangano la Abulahamu (w11 5/15 23 ¶13)

    • Aroma 11:17, 20, 21​—Odzozedwa omwe analumikizidwa kumtengo wophiphiritsa wa maolivi ayenera kupitiriza kukhala ndi chikhulupiriro (w11 5/15 24 ¶15)

    • Aroma 11:25, 26​—Chiwerengero chokwanira cha Aisiraeli auzimu ‘chidzapulumuka’ (w11 5/15 25 ¶19)

  • Kufufuza Mfundo Zothandiza: (8 min.)

    • Aroma 9:21-23​—N’chifukwa chiyani tiyenera kulola kuumbidwa ndi Yehova yemwe ndi Woumba Mbiya Wamkulu? (w13 6/15 25 ¶5)

    • Aroma 10:2​—N’chifukwa chiyani tiyenera kudziwa Mulungu molondola kuti tizimulambira movomerezeka? (it-1 1260 ¶2)

    • Kodi mwaphunzira zotani zokhudza Yehova pa kuwerenga Baibulo kwa mlungu uno?

    • Kodi ndi mfundo zina ziti zothandiza zimene mwapeza pa kuwerenga Baibulo kwa mlungu uno?

  • Kuwerenga Baibulo: (Osapitirira 4 min.) Aroma 10:1-15 (th phunziro 10)

KUPHUNZITSA MWALUSO MU UTUMIKI

  • Vidiyo ya Ulendo Wobwereza Wachiwiri: (5 min.) Onerani ndi kukambirana mfundo za m’vidiyoyi.

  • Ulendo Wobwereza Wachiwiri: (Osapitirira 3 min.) Gwiritsani ntchito chitsanzo cha ulendo wobwereza wachiwiri. (th phunziro 6)

  • Phunziro la Baibulo: (Osapitirira 5 min.) Yambani ndi chitsanzo cha ulendo wobwereza wachiwiri ndipo kenako yambitsani phunziro la Baibulo pogwiritsa ntchito buku la Zimene Baibulo Limaphunzitsa. (th phunziro 9)

MOYO WATHU WACHIKHRISTU

  • Nyimbo Na. 60

  • “Kuwonjezera Luso Lathu mu Utumiki​—Kusiya Kuphunzira ndi Munthu Yemwe Sakupita Patsogolo”: (15 min.) Nkhani yokambirana. Onerani vidiyo.

  • Phunziro la Baibulo la Mpingo: (30 min.) jy mutu 27

  • Mfundo Zimene Taphunzira Komanso za Mlungu Wamawa (3 min.)

  • Nyimbo Na. 57 ndi Pemphero

    Mabuku a Chichewa (1974-2025)
    Tulukani
    Lowani
    • Chichewa
    • Tumizirani Ena
    • Zimene Mumakonda
    • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
    • Zoyenera Kutsatira
    • Nkhani Yosunga Chinsinsi
    • Privacy Settings
    • JW.ORG
    • Lowani
    Tumizirani Ena