September 16-22
AHEBERI 11
Nyimbo Na. 119 ndi Pemphero
Mawu Oyamba (Osapitirira 3 min.)
CHUMA CHOPEZEKA M’MAWU A MULUNGU
“Chikhulupiriro ndi Chofunika Kwambiri”: (10 min.)
Aheb. 11:1—Kodi chikhulupiriro chimatanthauza chiyani? (w16.10 27 ¶6)
Aheb. 11:6—Chikhulupiriro n’chofunika kuti tizikondweretsa Mulungu (w13 11/1 11 ¶2-5)
Aheb. 11:33-38—Chikhulupiriro chinathandiza atumiki akale a Mulungu kupirira mayesero omwe ankakumana nawo (w16.10 23 ¶10-11)
Kufufuza Mfundo Zothandiza: (8 min.)
Aheb. 11:4—Kodi n’chiyani chinathandiza Abele kukhala ndi chikhulupiriro cholimba? (it-1 804 ¶5)
Aheb. 11:5—Kodi Inoki anadalitsidwa bwanji chifukwa cha chikhulupiriro chake? (wp17.1 12-13)
Kodi mwaphunzira zotani zokhudza Yehova pa kuwerenga Baibulo kwa mlungu uno?
Kodi ndi mfundo zina ziti zothandiza zimene mwapeza pa kuwerenga Baibulo kwa mlungu uno?
Kuwerenga Baibulo: (Osapitirira 4 min.) Aheb. 11:1-16 (th phunziro 10)
KUPHUNZITSA MWALUSO MU UTUMIKI
Vidiyo ya Ulendo Wobwereza Woyamba: (5 min.) Onerani ndi kukambirana mfundo za m’vidiyoyi.
Ulendo Wobwereza Woyamba: (Osapitirira 3 min.) Gwiritsani ntchito chitsanzo cha ulendo wobwereza woyamba. (th phunziro 3)
Ulendo Wobwereza Woyamba: (Osapitirira 5 min.) Yambani ndi chitsanzo cha ulendo wobwereza woyamba. M’patseni kapepala komuitanira kumisonkhano yathu, kenako yerekezerani kumuonetsa vidiyo yakuti Kodi pa Nyumba ya Ufumu Pamachitika Zotani? (th phunziro 11)
MOYO WATHU WACHIKHRISTU
“Kodi Mudzatani pa Nthawi ya Chilala?”: (15 min.) Nkhani yokambirana. Onerani vidiyoyi.
Phunziro la Baibulo la Mpingo: (30 min.) jy mutu 51
Mfundo Zimene Taphunzira Komanso za Mlungu Wamawa (3 min.)
Nyimbo Na. 122 ndi Pemphero