CHUMA CHOPEZEKA M’MAWU A MULUNGU | AHEBERI 11
Chikhulupiriro ndi Chofunika Kwambiri
Kodi chikhulupiriro cholimba chingakuthandizeni bwanji pa zochitika zotsatirazi?
Ngati mutapatsidwa utumiki wovuta kwambiri.—Aheb. 11:8-10
Ngati munthu amene mumamukonda wamwalira.—Aheb. 11:17-19
Ngati akuluakulu a boma ataletsa kulambira kwathu.—Aheb. 11:23-26