Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • mwb20 April tsamba 6
  • Kuopsa Kocheza ndi Anthu a Makhalidwe Oipa

Palibe Vidiyo.

Pepani vidiyoyi ikukanika kutsegula.

  • Kuopsa Kocheza ndi Anthu a Makhalidwe Oipa
  • Utumiki Komanso Moyo Wathu Wachikhristu—Ndandanda ya Misonkhano—2020
  • Nkhani Yofanana
  • Kukambirana Nkhani Zauzimu Kumalimbikitsa
    Nsanja ya Olonda—2003
  • Chisonkhezero cha Mabwenzi ndi Mwayi Wanu Wolalikira
    Utumiki Wathu wa Ufumu—2000
  • Muzicheza ndi Anthu Amene Amakonda Yehova
    Utumiki Komanso Moyo Wathu wa Chikhristu—Ndandanda ya Misonkhano—2019
  • Muzikonda Anthu Amene Mulungu Amawakonda
    Kodi Mungatani Kuti ‘Mulungu Apitirize Kukukondani’?
Onani Zambiri
Utumiki Komanso Moyo Wathu Wachikhristu—Ndandanda ya Misonkhano—2020
mwb20 April tsamba 6
M’bale akumwa zakumwa ndi anzake akuntchito pambuyo poweruka ku ntchito. Iye akumva chisoni ndi zomwe anzakewo akukambirana zokhudza zomwe amakonda, monga zovala, masewera apakompyuta, ndalama, komanso zipangizo zamakono.

CHUMA CHOPEZEKA M’MAWU A MULUNGU | GENESIS 34-35

Kuopsa Kocheza ndi Anthu a Makhalidwe Oipa

34:1, 2, 7, 25

N’zoona kuti anthu ena monga oyandikana nawo nyumba, omwe timagwira nawo ntchito komanso anzathu akusukulu, angakhale ndi makhalidwe abwino. Komabe zimenezi siziwapangitsa kukhala anthu abwino kucheza nawo. Ndiye kodi n’chiyani chingakuthandizeni kudziwa anthu abwino ocheza nawo? Mungadzifunse kuti:

  • Kodi anthu amene ndimakonda kucheza nawo angandithandize kuti ndizikonda kwambiri Yehova?

  • Kodi zimene anzanga amakonda kunena zimasonyeza kuti chinthu chofunika kwambiri pamoyo wawo n’chiyani?​—Mt 12:34

DZIFUNSENI KUTI, ‘Kodi anthu amene ndimakonda kucheza nawo akundithandiza kuti ndizikonda kwambiri Yehova kapena ayi?’

    Mabuku a Chichewa (1974-2025)
    Tulukani
    Lowani
    • Chichewa
    • Tumizirani Ena
    • Zimene Mumakonda
    • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
    • Zoyenera Kutsatira
    • Nkhani Yosunga Chinsinsi
    • Privacy Settings
    • JW.ORG
    • Lowani
    Tumizirani Ena