Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • mwb20 April tsamba 6
  • April 27–May 3

Palibe Vidiyo.

Pepani vidiyoyi ikukanika kutsegula.

  • April 27–May 3
  • Utumiki Komanso Moyo Wathu Wachikhristu—Ndandanda ya Misonkhano—2020
Utumiki Komanso Moyo Wathu Wachikhristu—Ndandanda ya Misonkhano—2020
mwb20 April tsamba 6

April 27–May 3

GENESIS 34-35

  • Nyimbo Na. 28 ndi Pemphero

  • Mawu Oyamba (Osapitirira 1 min.)

CHUMA CHOPEZEKA M’MAWU A MULUNGU

  • “Kuopsa Kocheza ndi Anthu a Makhalidwe Oipa”: (10 min.)

    • Ge 34:1​—Dina ankakonda kucheza ndi atsikana achikanani (w97 2/1 30 ¶4)

    • Ge 34:2​—Sekemu anagwiririra Dina (lvs 124 ¶14)

    • Ge 34:7, 25​—Simiyoni ndi Levi anapha Sekemu komanso amuna onse a mumzinda wake (w09 9/1 21 ¶1-2)

  • Kufufuza Mfundo Zothandiza: (10 min.)

    • Ge 35:8​—Kodi Debora anali ndani, nanga tingaphunzire chiyani kwa iye? (it-1 600 ¶4)

    • Ge 35:22-26​—Kodi tikudziwa bwanji kuti si nthawi zonse pamene mwana woyamba kubadwa ankayenera kukhala mumzere wa makolo a Mesiya? (w17.12 14)

    • Kodi mwapeza mfundo ziti zokhudza Yehova, utumiki kapena zinthu zina pa kuwerenga Baibulo kwa mlungu uno?

  • Kuwerenga Baibulo: (Osapitirira 4 min.) Ge 34:1-19 (th phunziro 5)

KUPHUNZITSA MWALUSO MU UTUMIKI

  • Vidiyo ya Ulendo Wobwereza Wachiwiri: (5 min.) Nkhani yokambirana. Onerani vidiyoyi kenako funsani omvera mafunso otsatirawa: Kodi Elise anachita chiyani kuti amufike pamtima womvetsera wake? Kodi tingayambitse bwanji phunziro la Baibulo pogwiritsa ntchito buku la Zimene Baibulo Limaphunzitsa?

  • Ulendo Wobwereza Wachiwiri: (Osapitirira 3 min.) Gwiritsani ntchito chitsanzo cha ulendo wobwereza wachiwiri. (th phunziro 13)

  • Phunziro la Baibulo: (Osapitirira 5 min.) fg phunziro 4 ¶6-7 (th phunziro 14)

MOYO WATHU WACHIKHRISTU

  • Nyimbo Na. 40

  • “Chotsani Milungu Yachilendo”: (15 min.) Nkhani yokambirana. Onerani vidiyo yakuti “Tsutsani Mdyerekezi”.

  • Phunziro la Baibulo la Mpingo: (30 min.) jy mutu 82

  • Mfundo Zimene Taphunzira Komanso za Mlungu Wamawa (Osapitilira 3 min.)

  • Nyimbo Na. 83 ndi Pemphero

    Mabuku a Chichewa (1974-2025)
    Tulukani
    Lowani
    • Chichewa
    • Tumizirani Ena
    • Zimene Mumakonda
    • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
    • Zoyenera Kutsatira
    • Nkhani Yosunga Chinsinsi
    • Privacy Settings
    • JW.ORG
    • Lowani
    Tumizirani Ena