July 20-26
EKISODO 10-11
Nyimbo Na. 65 ndi Pemphero
Mawu Oyamba (1 min.)
CHUMA CHOPEZEKA M’MAWU A MULUNGU
“Mose ndi Aroni Anasonyeza Kulimba Mtima Kwambiri”: (10 min.)
Eks 10:3-6—Mose ndi Aroni anauza Farao molimba mtima za mliri wa 8 (w09 7/15 20 ¶6)
Eks 10:24-26—Mose ndi Aroni anakana kumvera Farao
Eks 10:28; 11:4-8—Mose ndi Aroni anauza Farao mopanda mantha za mliri wa 10 (it-2 436 ¶4)
Kufufuza Mfundo Zothandiza: (10 min.)
Eks 10:1, 2—Kodi makolo angaphunzire chiyani pa mavesiwa? (w95 9/1 11 ¶11)
Eks 11:7—Kodi Yehova ankatanthauza chiyani pamene ananena kuti “galu sadzauwa aliyense wa ana a Isiraeli”? (it-1 783 ¶5)
Pa kuwerenga Baibulo kwa mlungu uno, kodi mwapeza mfundo ziti zokhudza Yehova, utumiki kapena zinthu zina?
Kuwerenga Baibulo: (Osapitirira 4 min.) Eks 10:1-15 (th phunziro 10)
KUPHUNZITSA MWALUSO MU UTUMIKI
Vidiyo ya Ulendo Wobwereza: (5 min.) Nkhani yokambirana. Onerani vidiyoyi. Kenako funsani mafunso otsatirawa: Kodi mwaphunzira chiyani pa zimene wofalitsayu anakambirana ndi mwininyumba? Kodi wofalitsayu akanatani kuti agawire buku kapena kabuku kopezeka pa Zinthu Zophunzitsira?
Ulendo Wobwereza: (Osapitirira 4 min.) Yambani ndi chitsanzo cha ulendo wobwereza. Kenako muitanireni kumisonkhano yathu. (th phunziro 8)
Ulendo Wobwereza: (Osapitirira 4 min.) Yambani ndi chitsanzo cha ulendo wobwereza. Kenako mugawireni buku kapena kabuku kopezeka pa Zinthu Zophunzitsira. (th phunziro 12)
MOYO WATHU WACHIKHRISTU
“Kodi Zinthu za M’chilengedwe Zimatiphunzitsa Chiyani pa Nkhani ya Kulimba Mtima?”: (15 min.) Nkhani yokambirana. Onerani vidiyo yakuti Phunzirani Kulimba Mtima Kuchokera ku Zinthu za M’chilengedwe.
Phunziro la Baibulo la Mpingo: (30 min.) jy mutu 92
Mfundo Zimene Taphunzira Komanso za Mlungu Wamawa (3 min.)
Nyimbo Na. 43 ndi Pemphero