July Ndandanda ya Utumiki Komanso Moyo Wathu Wachikhristu ya July 2020 Zimene Tinganene July 6-12 CHUMA CHOPEZEKA M’MAWU A MULUNGU | EKISODO 6-7 “Tsopano Uona Zimene Ndichite kwa Farao” July 13-19 CHUMA CHOPEZEKA M’MAWU A MULUNGU | EKISODO 8-9 Farao Yemwe Anali Wonyada Anathandiza Kukwaniritsa Cholinga cha Mulungu Mosadziwa MOYO WATHU WACHIKHRISTU Muzidzichepetsa—Muzipewa Kudzitama MOYO WATHU WACHIKHRISTU Muzidzichepetsa Ena Akamakuyamikirani July 20-26 CHUMA CHOPEZEKA M’MAWU A MULUNGU | EKISODO 10-11 Mose ndi Aroni Anasonyeza Kulimba Mtima Kwambiri MOYO WATHU WACHIKHRISTU Kodi Zinthu za M’chilengedwe Zimatiphunzitsa Chiyani pa Nkhani ya Kulimba Mtima? July 27–August 2, 2020 CHUMA CHOPEZEKA M’MAWU A MULUNGU | EKISODO 12 Kufunika kwa Mwambo wa Pasika kwa Akhristu MOYO WATHU WACHIKHRISTU Yehova Amateteza Anthu Ake