August 17-23
EKISODO 17-18
Nyimbo Na. 79 ndi Pemphero
Mawu Oyamba (1 min.)
CHUMA CHOPEZEKA M’MAWU A MULUNGU
“Amuna Odzichepetsa Amaphunzitsa Ena N’kumawapatsa Zochita”: (10 min.)
Eks 18:17, 18—Yetero anazindikira kuti Mose anali ndi udindo waukulu (w13 2/1 6)
Eks 18:21, 22—Yetero analimbikitsa Mose kuti apereke ntchito zina kwa amuna ena oyenerera (w03 11/1 6 ¶1)
Eks 18:24, 25—Mose anatsatira malangizo a Yetero (w02 5/15 25 ¶6)
Kufufuza Mfundo Zothandiza: (10 min.)
Eks 17:11-13—Kodi tingatsanzire bwanji Aroni ndi Hura amene anachita zinthu mwamsanga kuti athandize Mose? (w16.09 6 ¶14)
Eks 17:14—N’chifukwa chiyani mabuku amene Mose analemba ali m’gulu la mabuku ovomerezeka a m’Baibulo? (it-1 406)
Pa kuwerenga Baibulo kwa mlungu uno, kodi mwapeza mfundo ziti zokhudza Yehova, utumiki kapena zinthu zina?
Kuwerenga Baibulo: (Osapitirira 4 min.) Eks 17:1-16 (th phunziro 10)
KUPHUNZITSA MWALUSO MU UTUMIKI
Vidiyo ya Ulendo Wobwereza: (5 min.) Nkhani yokambirana. Onerani vidiyoyi. Kenako funsani omvera mafunso otsatirawa: Kodi tikuphunzira chiyani pa mmene Linda anayankhira Jamie atanena maganizo ake pa zimene zimachitika munthu akamwalira? Kodi Linda anachita chiyani pofuna kusonyeza kuti mfundo yapalembali ndi yothandiza?
Ulendo Wobwereza: (Osapitirira 3 min.) Gwiritsani ntchito chitsanzo cha ulendo wobwereza. (th phunziro 12)
Ulendo Wobwereza: (Osapitirira 4 min.) Yambani ndi chitsanzo cha ulendo wobwereza. Kenako gawirani buku la Zimene Baibulo Limaphunzitsa, ndipo yambitsani phunziro la Baibulo pogwiritsa ntchito mutu 6.(th phunziro 7)
MOYO WATHU WACHIKHRISTU
Zofunika Pampingo: (15 min.)
Phunziro la Baibulo la Mpingo: (30 min.) jy mutu 96
Mawu Omaliza (Osapitirira 3 min.)
Nyimbo Na. 136 ndi Pemphero