Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • mwb21 January tsamba 2
  • January 4-10

Palibe Vidiyo.

Pepani vidiyoyi ikukanika kutsegula.

  • January 4-10
  • Kabuku ka Msonkhano wa Utumiki Komanso Moyo Wathu Wachikhristu—2021
Kabuku ka Msonkhano wa Utumiki Komanso Moyo Wathu Wachikhristu—2021
mwb21 January tsamba 2

January 4-10

LEVITIKO 18-​19

  • Nyimbo Na. 122 ndi Pemphero

  • Mawu Oyamba (1 min.)

CHUMA CHOPEZEKA M’MAWU A MULUNGU

  • “Pitirizani Kukhala Ndi Makhalidwe Oyera”: (10 min.)

  • Mfundo Zothandiza: (10 min.)

    • Le 19:​9, 10​—Kodi Chilamulo chinkasonyeza bwanji kuti Mulungu amaganizira osauka? (w06 6/15 22 ¶11)

    • Pa kuwerenga Baibulo kwa mlungu uno, kodi mwapeza mfundo ziti zokhudza Yehova, utumiki kapena zinthu zina?

  • Kuwerenga Baibulo: (4 min.) Le 18:​1-15 (th phunziro 5)

KUPHUNZITSA MWALUSO MU UTUMIKI

  • Vidiyo ya Ulendo Woyamba: (5 min.) Nkhani yokambirana. Onerani vidiyo yakuti, Ulendo Woyamba: Pemphero​—Sl 65:2. Muziimitsa nthawi iliyonse imene pali chizindikiro chosonyeza kuti muime n’kufunsa omvera mafunso omwe ali m’vidiyoyi.

  • Ulendo Woyamba: (3 min.) Gwiritsani ntchito chitsanzo cha ulendo woyamba. (th phunziro 3)

  • Nkhani: (5 min.) w02 2/1 29​—Mutu: Kodi Malamulo Oletsa Ukwati Wapachibale Amene Ali M’Chilamulo cha Mose Amagwira Ntchito Bwanji kwa Akhristu Masiku Ano? (th phunziro 7)

MOYO WATHU WACHIKHRISTU

  • Nyimbo Na. 134

  • Khalani Bwenzi la Yehova​—Tetezani Ana Anu: (5 min.) Nkhani yokambidwa ndi mkulu. Onerani vidiyoyi. Kenako fotokozani zimene tikuphunzirapo.​—Miy 22:3.

  • “Makolo Muzithandiza Ana Anu Kukhala Odziwa Zinthu”: (10 min.) Nkhani yokambirana. Onerani vidiyo yakuti, Mangani Nyumba Yolimba​—Muziteteza Ana Anu ku “Zinthu Zoipa.”

  • Phunziro la Baibulo la Mpingo: (30 min.) jy mutu 115

  • Mawu Omaliza (3 min.)

  • Nyimbo Na. 124 ndi Pemphero

    Mabuku a Chichewa (1974-2025)
    Tulukani
    Lowani
    • Chichewa
    • Tumizirani Ena
    • Zimene Mumakonda
    • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
    • Zoyenera Kutsatira
    • Nkhani Yosunga Chinsinsi
    • Privacy Settings
    • JW.ORG
    • Lowani
    Tumizirani Ena