Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • mwb22 March tsamba 2
  • March 7-13

Palibe Vidiyo.

Pepani vidiyoyi ikukanika kutsegula.

  • March 7-13
  • Kabuku ka Msonkhano wa Utumiki Komanso Moyo Wathu Wachikhristu—2022
Kabuku ka Msonkhano wa Utumiki Komanso Moyo Wathu Wachikhristu—2022
mwb22 March tsamba 2

March 7-13

1 SAMUELI 12-13

  • Nyimbo Na. 4 ndi Pemphero

  • Mawu Oyamba (1 min.)

CHUMA CHOPEZEKA M’MAWU A MULUNGU

  • “Kudzikuza Kumabweretsa Manyazi”: (10 min.)

  • Mfundo Zothandiza: (10 min.)

    • 1Sa 12:21​—Kodi anthu ankatsatira bwanji zinthu ‘zopanda pake’? (w11 7/15 13 ¶15)

    • Pa kuwerenga Baibulo kwa mlungu uno, kodi mwapeza mfundo ziti zokhudza Yehova, utumiki kapena zinthu zina?

  • Kuwerenga Baibulo: (4 min.) 1Sa 12:1-11 (th phunziro 2)

KUPHUNZITSA MWALUSO MU UTUMIKI

  • Vidiyo ya Ulendo Woyamba: (5 min.) Nkhani yokambirana. Onerani vidiyo yakuti Ulendo Woyamba: Yesu​—Mt 16:16. Muziimitsa vidiyoyi nthawi iliyonse imene pali chizindikiro chosonyeza kuti muime n’kufunsa omvera mafunso omwe ali muvidiyoyi.

  • Ulendo Woyamba: (3 min.) Yambani ndi chitsanzo cha ulendo woyamba. Sonyezani mmene mungayankhire munthu amene wanena zinthu zina zomwe anthu amakonda kunena ngati sakufuna kuti tikambirane nawo. (th phunziro 1)

  • Phunziro la Baibulo: (5 min.) lff phunziro 04 mawu oyamba komanso mfundo 1-2 (th phunziro 13)

MOYO WATHU WACHIKHRISTU

  • Nyimbo Na. 46

  • Zimene Gulu Lathu Lachita: (5 min.) Onerani vidiyo ya Zimene Gulu Lathu Lachita ya March.

  • Zofunika Pampingo: (10 min.)

  • Phunziro la Baibulo la Mpingo: (30 min.) lvs mutu 13 ndime 1-12

  • Mawu Omaliza (3 min.)

  • Nyimbo Na. 87 ndi Pemphero

    Mabuku a Chichewa (1974-2025)
    Tulukani
    Lowani
    • Chichewa
    • Tumizirani Ena
    • Zimene Mumakonda
    • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
    • Zoyenera Kutsatira
    • Nkhani Yosunga Chinsinsi
    • Privacy Settings
    • JW.ORG
    • Lowani
    Tumizirani Ena