Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • mwb22 May tsamba 6
  • May 23-29

Palibe Vidiyo.

Pepani vidiyoyi ikukanika kutsegula.

  • May 23-29
  • Kabuku ka Msonkhano wa Utumiki Komanso Moyo Wathu Wachikhristu—2022
Kabuku ka Msonkhano wa Utumiki Komanso Moyo Wathu Wachikhristu—2022
mwb22 May tsamba 6

May 23-29

2 SAMUELI 4-6

  • Nyimbo Na. 135 ndi Pemphero

  • Mawu Oyamba (1 min.)

CHUMA CHOPEZEKA M’MAWU A MULUNGU

  • “Muzikhala Ndi Mantha Oyenera Poopa Kukhumudwitsa Yehova”: (10 min.)

  • Mfundo Zothandiza: (10 min.)

    • 2Sa 6:8, 9​—Kodi tikuphunzira chiyani pa zimene Davide anachita Yehova atakwiya? (w96 4/1 29 ¶1)

    • Pa kuwerenga Baibulo kwa mlungu uno, kodi mwapeza mfundo ziti zokhudza Yehova, utumiki kapena zinthu zina?

  • Kuwerenga Baibulo: (4min.) 2Sa 4:1-12 (th phunziro 10)

KUPHUNZITSA MWALUSO MU UTUMIKI

  • Ulendo Woyamba: (3 min.) Gwiritsani ntchito chitsanzo cha ulendo woyamba. Sonyezani mmene mungayankhire munthu amene wanena zinthu zomwe anthu amakonda kunena ngati sakufuna kuti tikambirane nawo. (th phunziro 12)

  • Ulendo Wobwereza: (4 min.) Yambani ndi chitsanzo cha ulendo wobwereza. Yerekezerani kumuonetsa vidiyo yakuti N’chifukwa Chiyani Tiyenera Kuphunzira Baibulo? (th phunziro 9)

  • Nkhani: (5 min.) w05 10/1 23-24 ¶14-15​—Mutu: “Opani Mulungu ndi Kumupatsa Ulemerero.”​—Chv 14:7. (th phunziro 19)

MOYO WATHU WACHIKHRISTU

  • Nyimbo Na. 143

  • “Kodi Mwakonzeka Kukumana ndi Zachiwawa?”: (15 min.) Nkhani yokambirana yokambidwa ndi mkulu. Onerani vidiyo yakuti Kodi Mwakonzeka Kukumana ndi Ngozi Zogwa Mwadzidzidzi?. Tchulaninso zilengezo zochokera ku ofesi ya nthambi kapena ku bungwe la akulu ngati zilipo.

  • Phunziro la Baibulo la Mpingo: (30 min.) lff phunziro 05

  • Mawu Omaliza (3 min.)

  • Nyimbo Na. 96 ndi Pemphero

    Mabuku a Chichewa (1974-2025)
    Tulukani
    Lowani
    • Chichewa
    • Tumizirani Ena
    • Zimene Mumakonda
    • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
    • Zoyenera Kutsatira
    • Nkhani Yosunga Chinsinsi
    • Privacy Settings
    • JW.ORG
    • Lowani
    Tumizirani Ena