Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • mwb22 September tsamba 11
  • October 17-23

Palibe Vidiyo.

Pepani vidiyoyi ikukanika kutsegula.

  • October 17-23
  • Kabuku ka Msonkhano wa Utumiki Komanso Moyo Wathu Wachikhristu—2022
Kabuku ka Msonkhano wa Utumiki Komanso Moyo Wathu Wachikhristu—2022
mwb22 September tsamba 11

October 17-23

1 MAFUMU 21-22

  • Nyimbo Na. 134 ndi Pemphero

  • Mawu Oyamba (1 min.)

CHUMA CHOPEZEKA M’MAWU A MULUNGU

  • “Muzitsanzira Mmene Yehova Amagwiritsira Ntchito Udindo Wake”: (10 min.)

  • Mfundo Zothandiza: (10 min.)

    • 1Mf 21:27-29​—Kodi tikudziwa bwanji kuti zochita za Ahabu sizinasonyeze kuti analapa kuchokera pansi pamtima? (w21.10 3 ¶4-6)

    • Pa kuwerenga Baibulo kwa mlungu uno, kodi mwapeza mfundo ziti zokhudza Yehova, utumiki kapena zinthu zina?

  • Kuwerenga Baibulo: (4 min.) 1Mf 22:24-38 (th phunziro 2)

KUPHUNZITSA MWALUSO MU UTUMIKI

  • Ulendo Woyamba: (3 min.) Yambani ndi nkhani imene ili mu chitsanzo cha ulendo woyamba. M’pempheni kuti muziphunzira naye Baibulo pogwiritsa ntchito kabuku kakuti Mungakhale Ndi Moyo Mpaka Kalekale. (th phunziro 4)

  • Ulendo Wobwereza: (4 min.) Yambani ndi nkhani imene ili mu chitsanzo cha ulendo wobwereza. Mugawireni kabuku kakuti Mungakhale Ndi Moyo Mpaka Kalekale ndipo yambitsani phunziro la Baibulo pogwiritsa ntchito phunziro 01. (th phunziro 6)

  • Nkhani: (5 min.) w15 3/15 9-11 ¶10-12​—Mutu: Kodi Tikuphunzira Chiyani pa Kukhulupirika kwa Naboti? (th phunziro 14)

MOYO WATHU WACHIKHRISTU

  • Nyimbo Na. 116

  • “Chikondi N’choleza Mtima Ndiponso N’chokoma Mtima”: (10 min.) Nkhani yokambirana. Onerani vidiyoyi. Kenako funsani omvera mafunso otsatirawa: Kodi a Alexandru anasonyeza bwanji kuleza mtima komanso kukoma mtima monga mutu wa banja? N’chifukwa chiyani a Dorina anasintha n’kupita kwa nthawi? Kodi tikuphunzira chiyani pa zimene zinachitikira banjali?

  • Zofunika Pampingo: (5 min.)

  • Phunziro la Baibulo la Mpingo: (30 min.) lff phunziro 23

  • Mawu Omaliza (3 min.)

  • Nyimbo Na. 50 ndi Pemphero

    Mabuku a Chichewa (1974-2025)
    Tulukani
    Lowani
    • Chichewa
    • Tumizirani Ena
    • Zimene Mumakonda
    • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
    • Zoyenera Kutsatira
    • Nkhani Yosunga Chinsinsi
    • Privacy Settings
    • JW.ORG
    • Lowani
    Tumizirani Ena