Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • mwb22 November tsamba 2
  • November 7-13

Palibe Vidiyo.

Pepani vidiyoyi ikukanika kutsegula.

  • November 7-13
  • Kabuku ka Msonkhano wa Utumiki Komanso Moyo Wathu Wachikhristu—2022
Kabuku ka Msonkhano wa Utumiki Komanso Moyo Wathu Wachikhristu—2022
mwb22 November tsamba 2

November 7-13

2 MAFUMU 5-6

  • Nyimbo Na. 55 ndi Pemphero

  • Mawu Oyamba (1 min.)

CHUMA CHOPEZEKA M’MAWU A MULUNGU

  • “Tili Ndi Ambiri Kuposa Amene Ali Ndi Iwowo”: (10 min.)

  • Mfundo Zothandiza: (10 min.)

    • 2Mf 5:15, 16​—N’chifukwa chiyani Elisa anakana mphatso ya Namani? (w05 8/1 9 ¶2)

    • Pa kuwerenga Baibulo kwa mlungu uno, kodi mwapeza mfundo ziti zokhudza Yehova, utumiki kapena zinthu zina?

  • Kuwerenga Baibulo: (4 min.) 2Mf 5:1-14 (th phunziro 2)

KUPHUNZITSA MWALUSO MU UTUMIKI

  • Vidiyo ya Ulendo Woyamba: (5 min.) Nkhani yokambirana. Onerani vidiyo ya Ulendo Woyamba: Uthenga Wabwino​—Sl 37:10, 11. Muziimitsa vidiyoyi nthawi iliyonse imene pali chizindikiro chosonyeza kuti muime n’kufunsa omvera mafunso omwe ali muvidiyoyi.

  • Ulendo Woyamba: (3 min.) Yambani ndi nkhani imene ili mu chitsanzo cha ulendo woyamba. Sonyezani mmene mungayankhire munthu amene wanena zinthu zomwe anthu amakonda kunena ngati sakufuna kuti tikambirane nawo. (th phunziro 12)

  • Phunziro la Baibulo: (5 min.) lff phunziro 08 mawu oyamba komanso mfundo 1-3 (th phunziro 15)

MOYO WATHU WACHIKHRISTU

  • Nyimbo Na. 37

  • “Khalani Opatsa”: (15 min.) Nkhani yokambirana yokambidwa ndi mkulu. Onerani vidiyo yakuti Tikukuthokozani Chifukwa cha Mtima Wanu Wopatsa. Ayamikireni abale ndi alongo chifukwa cha zinthu zosiyanasiyana zimene amachita zosonyeza kuti ali ndi mtima wopatsa.

  • Phunziro la Baibulo la Mpingo: (30 min.) lff phunziro 26

  • Mawu Omaliza (3 min.)

  • Nyimbo Na. 30 ndi Pemphero

    Mabuku a Chichewa (1974-2025)
    Tulukani
    Lowani
    • Chichewa
    • Tumizirani Ena
    • Zimene Mumakonda
    • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
    • Zoyenera Kutsatira
    • Nkhani Yosunga Chinsinsi
    • Privacy Settings
    • JW.ORG
    • Lowani
    Tumizirani Ena