Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • mwb23 January tsamba 4
  • January 16-22

Palibe Vidiyo.

Pepani vidiyoyi ikukanika kutsegula.

  • January 16-22
  • Utumiki Komanso Moyo Wathu Wachikhristu—2023
Utumiki Komanso Moyo Wathu Wachikhristu—2023
mwb23 January tsamba 4

January 16-22

1 MBIRI 1-3

  • Nyimbo Na. 96 ndi Pemphero

  • Mawu Oyamba (1 min.)

CHUMA CHOPEZEKA M’MAWU A MULUNGU

  • “Baibulo Ndi Buku Limene Limanena Zoona”: (10 min.)

  • Mfundo Zothandiza: (10 min.)

    • 1Mb 3:1-3​—N’chifukwa chiyani nthawi zina akazi ankatchulidwa m’Baibulo? (it-1 911 ¶3-4)

    • Pa kuwerenga Baibulo kwa mlungu uno, kodi mwapeza mfundo ziti zokhudza Yehova, utumiki kapena zinthu zina?

  • Kuwerenga Baibulo: (4 min.) 1Mb 1:43-54 (th phunziro 5)

KUPHUNZITSA MWALUSO MU UTUMIKI

  • Ulendo Woyamba: (3 min.) Yambani ndi nkhani imene ili mu chitsanzo cha ulendo woyamba. Gawirani magazini yomwe ili ndi nkhani imene mwininyumba anatchula. (th phunziro 4)

  • Ulendo Wobwereza: (4 min.) Yambani ndi nkhani imene ili mu chitsanzo cha ulendo wobwereza. Mugawireni chimodzi mwa Zinthu Zophunzitsira. (th phunziro 1)

  • Phunziro la Baibulo: (5 min.) lff phunziro 08 mfundo 7 komanso Zimene Ena Amanena (th phunziro 8)

MOYO WATHU WACHIKHRISTU

  • Nyimbo Na. 98

  • “Muzikhulupirira Kwambiri Mawu a Mulungu”: (15 min.) Nkhani yokambirana komanso vidiyo.

  • Phunziro la Baibulo la Mpingo: (30 min.) lff phunziro 34

  • Mawu Omaliza (3 min.)

  • Nyimbo Na. 89 ndi Pemphero

    Mabuku a Chichewa (1974-2025)
    Tulukani
    Lowani
    • Chichewa
    • Tumizirani Ena
    • Zimene Mumakonda
    • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
    • Zoyenera Kutsatira
    • Nkhani Yosunga Chinsinsi
    • Privacy Settings
    • JW.ORG
    • Lowani
    Tumizirani Ena