Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • mwb23 May tsamba 11
  • June 12-18

Palibe Vidiyo.

Pepani vidiyoyi ikukanika kutsegula.

  • June 12-18
  • Utumiki Komanso Moyo Wathu Wachikhristu—2023
Utumiki Komanso Moyo Wathu Wachikhristu—2023
mwb23 May tsamba 11

June 12-18

2 MBIRI 32-33

  • Nyimbo Na. 103 ndi Pemphero

  • Mawu Oyamba (1 min.)

CHUMA CHOPEZEKA M’MAWU A MULUNGU

  • “Muzilimbikitsa Abale ndi Alongo Anu Akakumana ndi Mavuto”: (10 min.)

  • Mfundo Zothandiza: (10 min.)

    • 2Mb 33:15, 16​—Kodi tingaphunzire chiyani pa chitsanzo cha Manase? (w21.10 4-5 ¶11-12)

    • Pa kuwerenga Baibulo kwa mlungu uno, kodi mwapeza mfundo ziti zokhudza Yehova, utumiki kapena zinthu zina?

  • Kuwerenga Baibulo: (4 min.) 2Mb 32:1-15 (th phunziro 11)

KUPHUNZITSA MWALUSO MU UTUMIKI

  • Ulendo Woyamba: (4 min.) Kambiranani tsamba lomaliza la kabuku kakuti Mungakhale Ndi Moyo Mpaka Kalekale, ndipo m’pempheni kuti muziphunzira naye Baibulo. (th phunziro 6)

  • Ulendo Wobwereza: (3 min.) Yambani ndi nkhani imene ili mu chitsanzo cha ulendo wobwereza. Mugawireni chimodzi mwa Zinthu Zophunzitsira. (th phunziro 17)

  • Phunziro la Baibulo: (5 min.) lff phunziro 10 mfundo 5 (th phunziro 19)

MOYO WATHU WACHIKHRISTU

  • Nyimbo Na. 36

  • “Dzitetezeni kwa Anthu Ampatuko”: (10 min.) Nkhani yokambirana komanso vidiyo.

  • Zofunika Pampingo: (5 min.)

  • Phunziro la Baibulo la Mpingo: (30 min.) lff phunziro 48 mfundo 1-4

  • Mawu Omaliza (3 min.)

  • Nyimbo Na. 90 ndi Pemphero

    Mabuku a Chichewa (1974-2025)
    Tulukani
    Lowani
    • Chichewa
    • Tumizirani Ena
    • Zimene Mumakonda
    • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
    • Zoyenera Kutsatira
    • Nkhani Yosunga Chinsinsi
    • Privacy Settings
    • JW.ORG
    • Lowani
    Tumizirani Ena