Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • mwb23 September tsamba 14
  • October 30–November 5

Palibe Vidiyo.

Pepani vidiyoyi ikukanika kutsegula.

  • October 30–November 5
  • Utumiki Komanso Moyo Wathu Wachikhristu—2023
Utumiki Komanso Moyo Wathu Wachikhristu—2023
mwb23 September tsamba 14

October 30–November 5

YOBU 11-12

  • Nyimbo Na. 87 ndi Pemphero

  • Mawu Oyamba (1 min.)

CHUMA CHOPEZEKA M’MAWU A MULUNGU

  • “Njira Zitatu Zomwe Tingapezere Nzeru N’kumazigwiritsa Ntchito”: (10 min.)

  • Mfundo Zothandiza: (10 min.)

    • Yob 12:11—Kodi mfundo ya palembali ingatithandize bwanji kuti tizimvetsera bwino ena akamalankhula? (w08 8/1 11 ¶5)

    • Pa kuwerenga Baibulo kwa mlungu uno, kodi mwapeza mfundo ziti zokhudza Yehova, utumiki kapena zinthu zina?

  • Kuwerenga Baibulo: (4 min.) Yob 12:​1-25 (th phunziro 5)

KUPHUNZITSA MWALUSO MU UTUMIKI

  • Ulendo Woyamba: (4 min.) Yambani ndi nkhani imene ili mu chitsanzo cha ulendo woyamba. Muuzeni kuti timaphunzira Baibulo ndi anthu, ndipo musiyireni khadi lodziwitsa anthu za phunziro la Baibulo. (th phunziro 1)

  • Ulendo Wobwereza: (3 min.) Yambani ndi nkhani imene ili mu chitsanzo cha ulendo wobwereza. Muitanireni ku misonkhano yathu, ndipo yerekezerani kumuonetsa vidiyo yakuti Kodi pa Nyumba ya Ufumu Pamachitika Zotani?, kenako kambiranani naye mfundo za muvidiyoyi. (th phunziro 13)

  • Phunziro la Baibulo: (5 min.) lff phunziro 12 zomwe taphunzira, kubwereza komanso zolinga (th phunziro 19)

MOYO WATHU WACHIKHRISTU

  • Nyimbo Na. 135

  • “Makolo, Muzithandiza Ana Anu Kupeza Nzeru Zochokera kwa Mulungu”: (15 min.) Nkhani yokambirana komanso vidiyo.

  • Phunziro la Baibulo la Mpingo: (30 min.) bt mutu 1 ¶8-15 ndi bokosi patsamba 12

  • Mawu Omaliza (3 min.)

  • Nyimbo Na. 3 ndi Pemphero

    Mabuku a Chichewa (1974-2025)
    Tulukani
    Lowani
    • Chichewa
    • Tumizirani Ena
    • Zimene Mumakonda
    • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
    • Zoyenera Kutsatira
    • Nkhani Yosunga Chinsinsi
    • Privacy Settings
    • JW.ORG
    • Lowani
    Tumizirani Ena