November 27–December 3
YOBU 20-21
Nyimbo Na. 38 ndi Pemphero
Mawu Oyamba (1 min.)
CHUMA CHOPEZEKA M’MAWU A MULUNGU
“Chuma Sichipangitsa Munthu Kukhala Wolungama”: (10 min.)
Mfundo Zothandiza: (10 min.)
Yob 20:2—Kodi akulu angathandize bwanji anthu amene akulimbana ndi ‘maganizo osautsa’? (w95 1/1 9 ¶19)
Pa kuwerenga Baibulo kwa mlungu uno, kodi mwapeza mfundo ziti zokhudza Yehova, utumiki kapena zinthu zina?
Kuwerenga Baibulo: (4 min.) Yob 20:1-22 (th phunziro 5)
KUPHUNZITSA MWALUSO MU UTUMIKI
Ulendo Woyamba: (2 min.) Gwiritsani ntchito nkhani imene ili mu chitsanzo cha ulendo woyamba. (th phunziro 1)
Ulendo Wobwereza: (5 min.) Yambani ndi nkhani imene ili mu chitsanzo cha ulendo wobwereza. Mugawireni kabuku kakuti Mungakhale Ndi Moyo Mpaka Kalekale, ndipo musonyezeni mmene phunziro la Baibulo limachitikira. (th phunziro 6)
Nkhani: (5 min.) g 5/09 12-13—Mutu: Kodi Mulungu Amafuna Kuti Mukhale Wolemera? (th phunziro 17)
MOYO WATHU WACHIKHRISTU
“Mukhale Okhutira Ndi Zimene Muli Nazo Panopa”: (15 min.) Nkhani yokambirana komanso vidiyo.
Phunziro la Baibulo la Mpingo: (30 min.) bt mutu 2 ¶16-23
Mawu Omaliza (3 min.)
Nyimbo Na. 103 ndi Pemphero