December 18-24
YOBU 28-29
Nyimbo Na. 39 ndi Pemphero
Mawu Oyamba (1 min.)
CHUMA CHOPEZEKA M’MAWU A MULUNGU
“Kodi Muli ndi Mbiri Ngati ya Yobu?”: (10 min.)
Mfundo Zothandiza: (10 min.)
Yob 29:24—Kodi tingaphunzire chiyani pa chitsanzo cha Yobu? (g00 7/8 29 ¶3)
Pa kuwerenga Baibulo kwa mlungu uno, kodi mwapeza mfundo ziti zokhudza Yehova, utumiki kapena zinthu zina?
Kuwerenga Baibulo: (4 min.) Yob 28:1-28 (th phunziro 5)
KUPHUNZITSA MWALUSO MU UTUMIKI
Ulendo Woyamba: (3 min.) Yambani ndi nkhani imene ili mu chitsanzo cha ulendo woyamba. Mugawireni kabuku ka Mungakhale Ndi Moyo Mpaka Kalekale. (th phunziro 3)
Ulendo Wobwereza: (4 min.) Yambani ndi nkhani imene ili mu chitsanzo cha ulendo wobwereza. Mugawireni kabuku ka Mungakhale Ndi Moyo Mpaka Kalekale, kenako kambiranani mwachidule mbali yakuti “Zimene Mungachite Kuti Muzipindula ndi Phunziro Lililonse.” (th phunziro 17)
Phunziro la Baibulo: (5 min.) lff phunziro 13 mawu oyamba a pa Fufuzani Mozama ndi mfundo 4 (th phunziro 6)
MOYO WATHU WACHIKHRISTU
“Zochita Zanga Zimathandiza Kuti Gulu Lathu Likhale ndi Mbiri Yabwino”: (15 min.) Nkhani yokambirana komanso vidiyo.
Phunziro la Baibulo la Mpingo: (30 min.) bt mutu 3 ¶12-18
Mawu Omaliza (3 min.)
Nyimbo Na. 50 ndi Pemphero