Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • mwb25 January tsamba 4
  • January 13-19

Palibe Vidiyo.

Pepani vidiyoyi ikukanika kutsegula.

  • January 13-19
  • Utumiki Komanso Moyo Wathu wa Chikhristu—Kabuku ka Msonkhano—2025
Utumiki Komanso Moyo Wathu wa Chikhristu—Kabuku ka Msonkhano—2025
mwb25 January tsamba 4

JANUARY 13-19

MASALIMO 135-137

Nyimbo Na. 2 ndi Pemphero | Mawu Oyamba (1 min.)

CHUMA CHOPEZEKA M’MAWU A MULUNGU

Mose watambasula manja ake ndipo madzi a m’Nyanja Yofiira akugawanika. Aisiraeli komanso anthu ena amene sanali Aisiraeli akuyang’ana modabwa.

1. “Ambuye Wathu Ndi Wamkulu Kuposa Milungu Ina Yonse”

(10 min.)

Yehova wasonyeza kuti iye ndi amene amatsogolera chilengedwe chonse (Sl 135:5, 6; it-2 661 ¶4-5)

Amateteza anthu ake (Eks 14:29-31; Sl 135:14)

Amakhala nafe tikafooka (Sl 136:23; w21.11 6 ¶16)

2. Mfundo Zothandiza

(10 min.)

  • Sl 135:1, 5—N’chifukwa chiyani mawu akuti “Ya” nthawi zambiri amagwiritsidwa ntchito m’Baibulo? (it-1 1248)

  • Kodi ndi mfundo ziti zimene mwapeza pa kuwerenga Baibulo kwa mlungu uno?

3. Kuwerenga Baibulo

(4 min.) Sl 135:1-21 (th phunziro 11)

KUPHUNZITSA MWALUSO MU UTUMIKI

4. Ulendo Woyamba

(3 min.) KULALIKIRA MWAMWAYI. Uzanani kumene mumakhala komanso patsanani manambala a foni ndi munthu amene wasonyeza chidwi. (lmd phunziro 2 mfundo 4)

5. Ulendo Wobwereza

(4 min.) KUNYUMBA NDI NYUMBA. Muitanireni ku misonkhano yathu. (lmd phunziro 9 mfundo 4)

6. Kufotokoza Zimene Mumakhulupirira

(5 min.) Chitsanzo. ijwfq 7—Mutu: Kodi a Mboni za Yehova Ndi Akhristu? (th phunziro 12)

MOYO WATHU WA CHIKHRISTU

Nyimbo Na. 10

7. Zofunika Pampingo

(15 min.)

8. Phunziro la Baibulo la Mpingo

(30 min.) bt mutu 21 ¶1-7, bokosi patsamba 166

Mawu Omaliza (3 min.) | Nyimbo Na. 90 ndi Pemphero

    Mabuku a Chichewa (1974-2025)
    Tulukani
    Lowani
    • Chichewa
    • Tumizirani Ena
    • Zimene Mumakonda
    • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
    • Zoyenera Kutsatira
    • Nkhani Yosunga Chinsinsi
    • Privacy Settings
    • JW.ORG
    • Lowani
    Tumizirani Ena