Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • mwb25 January tsamba 10-11
  • February 10-16

Palibe Vidiyo.

Pepani vidiyoyi ikukanika kutsegula.

  • February 10-16
  • Utumiki Komanso Moyo Wathu wa Chikhristu—Kabuku ka Msonkhano—2025
Utumiki Komanso Moyo Wathu wa Chikhristu—Kabuku ka Msonkhano—2025
mwb25 January tsamba 10-11

FEBRUARY 10-16

MASALIMO 147-150

Nyimbo Na. 12 ndi Pemphero | Mawu Oyamba (1 min.)

CHUMA CHOPEZEKA M’MAWU A MULUNGU

Wolemba masalimo akuyang’ana kumwamba kumene kuli nyenyezi ndipo akutamanda Yehova. Kachisi wa ku Yerusalemu akuoneka chapafupi.

1. Tili Ndi Zifukwa Zambiri Zotamandira Ya

(10 min.)

Iye amasamalira aliyense payekha (Sl 147:3, 4; w17.07 18 ¶5-6)

Iye ndi wachifundo ndipo amagwiritsa ntchito mphamvu zake kuti atithandize (Sl 147:5; w17.07 18 ¶7)

Iye anatipatsa mwayi wokhala m’gulu la anthu ake (Sl 147:19, 20; w17.07 21 ¶18)


DZIFUNSENI KUTI, ‘Kodi n’chiyaninso chimandilimbikitsa kuti ndizitamanda Yehova?’

2. Mfundo Zothandiza

(10 min.)

  • Sl 148:1, 10—Kodi mbalame zimatamanda bwanji Yehova? (it-1 316)

  • Kodi ndi mfundo ziti zimene mwapeza pa kuwerenga Baibulo kwa mlungu uno?

3. Kuwerenga Baibulo

(4 min.) Sl 148:1–149:9 (th phunziro 11)

KUPHUNZITSA MWALUSO MU UTUMIKI

4. Ulendo Woyamba

(3 min.) KUNYUMBA NDI NYUMBA. Mwininyumba wakuuzani kuti akudwala matenda okhalitsa. (lmd phunziro 2 mfundo 5)

5. Ulendo Woyamba

(4 min.) KULALIKIRA MWAMWAYI. Pezani mwayi woti mumuuze zomwe mwaphunzira kumisonkhano yaposachedwapa. (lmd phunziro 4 mfundo 3)

6. Nkhani

(5 min.) w19.03 10 ¶7-11—Mutu: Muzimvera Yesu—Muzilalikira Uthenga Wabwino. Onani chithunzi. (th phunziro 14)

Mwamuna ndi mkazi wake akulalikira bambo wina m’mbali mwa nyanja.

MOYO WATHU WA CHIKHRISTU

Nyimbo Na. 159

7. Lipoti la Chaka cha Utumiki

(15 min.) Nkhani yokambirana.

Pambuyo powerenga chilengezo chochokera ku ofesi ya nthambi chokhudza lipoti la chaka cha utumiki, funsani omvera kuti afotokoze zinthu zabwino zomwe zili mu Lipoti la Chaka cha Utumiki cha 2024 la Mboni za Yehova Padziko Lonse. Funsani ofalitsa omwe munawasankhiratu kuti afotokoze zinthu zolimbikitsa zimene anakumana nazo mu utumiki chaka chathachi.

Abale ndi alongo akulalikira m’malo osiyanasiyana padziko lonse. Akulalikira pogwiritsa ntchito timashelefu, vidiyokomfelensi, kunyumba ndi nyumba komanso njira zina.

8. Phunziro la Baibulo la Mpingo

(30 min.) bt mutu 22 ¶7-14, bokosi patsamba 174, 177

Mawu Omaliza (3 min.) | Nyimbo Na. 37 ndi Pemphero

    Mabuku a Chichewa (1974-2025)
    Tulukani
    Lowani
    • Chichewa
    • Tumizirani Ena
    • Zimene Mumakonda
    • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
    • Zoyenera Kutsatira
    • Nkhani Yosunga Chinsinsi
    • Privacy Settings
    • JW.ORG
    • Lowani
    Tumizirani Ena