Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • mwb25 March tsamba 3
  • March 10-16

Palibe Vidiyo.

Pepani vidiyoyi ikukanika kutsegula.

  • March 10-16
  • Utumiki Komanso Moyo Wathu wa Chikhristu—Kabuku ka Msonkhano—2025
Utumiki Komanso Moyo Wathu wa Chikhristu—Kabuku ka Msonkhano—2025
mwb25 March tsamba 3

MARCH 10-16

MIYAMBO 4

Nyimbo Na. 36 ndi Pemphero | Mawu Oyamba (1 min.)

CHUMA CHOPEZEKA M’MAWU A MULUNGU

Alonda akuchita zinthu mwamsanga pamene aona kuti kukubwera adani.

Mlonda yemwe ali pa nsanja akuuza alonda amene ali pansi kuti atseke geti lolowera mumzinda

1. “Muziteteza Mtima Wanu”

(10 min.)

Mawu akuti “mtima” amatanthauza munthu wamkati (Sl 51:6; w19.01 15 ¶4)

Chinthu chofunika kwambiri pa moyo wathu chiyenera kukhala kuteteza mtima wathu (Miy 4:23a; w19.01 17 ¶10-11; 18 ¶14; onani chithunzi)

Kuti tikhalebe ndi moyo zimadalira kuti mtima wathu wophiphiritsa uli bwanji (Miy 4:23b; w12 5/1 32 ¶2)

M’bale akuyang’ana kumbali pamene pafoni yake pabwera zinthu zosayenera.

2. Mfundo Zothandiza

(10 min.)

  • Miy 4:18—Kodi vesili likutithandiza bwanji kumvetsa mmene Mkhristu amasinthira zinthu pa moyo wake n’cholinga choti akhale pa ubwenzi ndi Yehova? (w21.08 8 ¶4)

  • Kodi ndi mfundo ziti zimene mwapeza pa kuwerenga Baibulo kwa mlungu uno?

3. Kuwerenga Baibulo

(4 min.) Miy 4:1-18 (th phunziro 12)

KUPHUNZITSA MWALUSO MU UTUMIKI

4. Ulendo Woyamba

(3 min.) KUNYUMBA NDI NYUMBA. Munthu wasonyeza chidwi mutamuitanira ku Chikumbutso. (lmd phunziro 1 mfundo 5)

5. Ulendo Woyamba

(4 min.) KULALIKIRA MWAMWAYI. Itanirani mnzanu ku Chikumbutso. (lmd phunziro 2 mfundo 3)

6. Kufotokoza Zimene Mumakhulupirira

(5 min.) Chitsanzo. ijwfq nkhani na. 19—Mutu: N’chifukwa Chiyani Simukondwerera Isitala? (lmd phunziro 3 mfundo 4)

MOYO WATHU WA CHIKHRISTU

Nyimbo Na. 16

7. Vidiyo ya Zimene Gulu Lathu Lachita ya March

(10 min.) Onerani VIDIYOYI.

8. Ntchito Yoitanira Anthu ku Chikumbutso Iyamba Loweruka pa 15 March

(5 min.) Nkhani yokambidwa ndi woyang’anira utumiki. Fotokozani zimene mpingo wanu wakonza zokhudza kugwira ntchitoyi, kumvetsera nkhani yapadera komanso mwambo wa Chikumbutso. Limbikitsani onse kuti ayesetse kuchita zambiri mu utumiki m’miyezi ya March ndi April.

9. Phunziro la Baibulo la Mpingo

(30 min.) bt mutu 23 ¶16-19, bokosi patsamba 188

Mawu Omaliza (3 min.) | Nyimbo Na. 76 ndi Pemphero

    Mabuku a Chichewa (1974-2025)
    Tulukani
    Lowani
    • Chichewa
    • Tumizirani Ena
    • Zimene Mumakonda
    • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
    • Zoyenera Kutsatira
    • Nkhani Yosunga Chinsinsi
    • Privacy Settings
    • JW.ORG
    • Lowani
    Tumizirani Ena