MARCH 31–APRIL 6
MIYAMBO 7
Nyimbo Na. 34 ndi Pemphero | Mawu Oyamba (1 min.)
1. Muzipewa Zochitika Zimene Zingakuikeni M’mayesero
(10 min.)
Mnyamata wosadziwa zinthu anapita mwadala kukayendayenda m’dera limene mumakhala mahule (Miy 7:7-9; w00 11/15 29 ¶5)
Hule akubwera kudzakumana naye kuti amukope (Miy 7:10, 13-21; w00 11/15 30 ¶4-6)
Iye akukumana ndi mavuto chifukwa chodziika m’mayesero mwadala (Miy 7:22, 23; w00 11/15 31 ¶2)
2. Mfundo Zothandiza
(10 min.)
Miy 7:3—Kodi kumanga malamulo a Mulungu kuzala zathu komanso kuwalemba pamtima pathu kumatanthauza chiyani? (w00 11/15 29 ¶1)
Kodi ndi mfundo ziti zimene mwapeza pa kuwerenga Baibulo kwa mlungu uno?
3. Kuwerenga Baibulo
(4 min.) Miy 7:6-20 (th phunziro 2)
4. Ulendo Wobwereza
(4 min.) KUNYUMBA NDI NYUMBA. Pa ulendo wapita, munthuyo analandira kapepala komuitanira ku Chikumbutso ndipo anasonyeza chidwi. (lmd phunziro 9 mfundo 5)
5. Ulendo Wobwereza
(4 min.) KULALIKIRA MWAMWAYI. Pamene munkalankhula ndi munthuyo pa ulendo wapita, analandira kapepala komuitanira ku Chikumbutso ndipo anasonyeza chidwi. (lmd phunziro 9 mfundo 4)
6. Ulendo Wobwereza
(4 min.) KULALIKIRA M’MALO OPEZEKA ANTHU AMBIRI. Pamene munkalankhula ndi munthuyo pa ulendo wapita, analandira kapepala komuitanira ku Chikumbutso ndipo anasonyeza chidwi. (lmd phunziro 9 mfundo 3)
Nyimbo Na. 13
7. Mpaka Nthawi Ina Yabwino (Lu 4:6)
(15 min.) Nkhani yokambirana.
Onerani VIDIYO. Kenako funsani mafunso otsatirawa:
Kodi Yesu anayesedwa bwanji, nanga ifeyo tingakumanenso bwanji ndi mayesero ofanana ndi amenewa?
Kodi tingakane bwanji mayesero a Mdyerekezi?
8. Phunziro la Baibulo la Mpingo
(30 min.) bt mutu 24 ¶13-21