Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • mwb25 March tsamba 11
  • April 14-20

Palibe Vidiyo.

Pepani vidiyoyi ikukanika kutsegula.

  • April 14-20
  • Utumiki Komanso Moyo Wathu wa Chikhristu—Kabuku ka Msonkhano—2025
Utumiki Komanso Moyo Wathu wa Chikhristu—Kabuku ka Msonkhano—2025
mwb25 March tsamba 11

APRIL 14-20

MIYAMBO 9

Nyimbo Na. 56 ndi Pemphero | Mawu Oyamba (1 min.)

CHUMA CHOPEZEKA M’MAWU A MULUNGU

1. Mukhale Anzeru, Osati Onyoza

(10 min.)

Munthu wonyoza amakana kulandira malangizo achikondi ndipo amakwiyira munthu amene akumupatsa malangizoyo (Miy 9:7, 8a; w22.02 9 ¶4)

Munthu wanzeru amayamikira malangizo komanso wopereka malangizoyo (Miy 9:8b, 9; w22.02 12 ¶12-14; w01 5/15 30 ¶1-2)

Munthu wanzeru adzapindula ndi nzeruzo, koma wonyoza adzavutika (Miy 9:12; w01 5/15 30 ¶5)

Mlongo wachitsikana akumvetsera mlongo wachikulire pamene akudya limodzi pa lesitilanti.

2. Mfundo Zothandiza

(10 min.)

  • Miy 9:17—Kodi “madzi akuba” n’chiyani, nanga n’chifukwa chiyani “amatsekemera”? (w06 9/15 17 ¶5)

  • Kodi ndi mfundo ziti zimene mwapeza pa kuwerenga Baibulo kwa mlungu uno?

3. Kuwerenga Baibulo

(4 min.) Miy 9:1-18 (th phunziro 5)

KUPHUNZITSA MWALUSO MU UTUMIKI

4. Ulendo Wobwereza

(4 min.) KUNYUMBA NDI NYUMBA. Munthuyo anabwera ku Chikumbutso. (lmd phunziro 8 mfundo 3)

5. Ulendo Wobwereza

(4 min.) KULALIKIRA M’MALO OPEZEKA ANTHU AMBIRI. Munthuyo munamuthandizapo kupeza malo amene kukachitikire Chikumbutso kufupi ndi kwawo. (lmd phunziro 7 mfundo 4)

6. Ulendo Wobwereza

(4 min.) KULALIKIRA MWAMWAYI. Munathandizapo wachibale wanu kupeza malo amene kukachitikire Chikumbutso kufupi ndi kwawo. (lmd phunziro 8 mfundo 4)

MOYO WATHU WA CHIKHRISTU

Nyimbo Na. 84

7. Kodi Mwayi wa Utumiki Umakuchititsani Kukhala Apadera?

(15 min.) Nkhani yokambirana.

Onerani VIDIYO. Kenako funsani mafunso otsatirawa:

  • Kodi mawu akuti “utumiki” amatanthauza chiyani?

  • Kodi anthu amene ali ndi maudindo mumpingo ayenera kumadziona bwanji?

  • N’chifukwa chiyani kutumikira ena n’kofunika kwambiri kuposa kulamulira ena?

8. Phunziro la Baibulo la Mpingo

(30 min.) bt mutu 25 ¶5-7, bokosi patsamba 200

Mawu Omaliza (3 min.) | Nyimbo Na. 42 ndi Pemphero

    Mabuku a Chichewa (1974-2025)
    Tulukani
    Lowani
    • Chichewa
    • Tumizirani Ena
    • Zimene Mumakonda
    • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
    • Zoyenera Kutsatira
    • Nkhani Yosunga Chinsinsi
    • Privacy Settings
    • JW.ORG
    • Lowani
    Tumizirani Ena