Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • mwb25 March tsamba 12-13
  • April 21-27

Palibe Vidiyo.

Pepani vidiyoyi ikukanika kutsegula.

  • April 21-27
  • Utumiki Komanso Moyo Wathu wa Chikhristu—Kabuku ka Msonkhano—2025
Utumiki Komanso Moyo Wathu wa Chikhristu—Kabuku ka Msonkhano—2025
mwb25 March tsamba 12-13

APRIL 21-27

MIYAMBO 10

Nyimbo Na. 76 ndi Pemphero | Mawu Oyamba (1 min.)

CHUMA CHOPEZEKA M’MAWU A MULUNGU

1. Kodi N’chiyani Chimathandiza Munthu Kumasangalaladi pa Moyo?

(10 min.)

Munthu amene amakhaladi wosangalala ndi amene amagwira ntchito mwakhama pothandiza ena kudziwa za Yehova (Miy 10:4, 5; w01 7/15 25 ¶1-3)

Kukhala wolungama n’kofunika kwambiri kuposa chuma (Miy 10:15, 16; w01 9/15 24 ¶3-4)

Munthu amene amadalitsidwa ndi Yehova ndi amene amakhaladi wosangalala (Miy 10:22; it-1 340)

Alongo awiri akuhagana pamsonkhano.

2. Mfundo Zothandiza

(10 min.)

  • Miy 10:22—N’chifukwa chiyani atumiki a Mulungu amakumana ndi mavuto ambiri chonsecho madalitso a Yehova sawonjezerapo ululu? (w06 5/15 30 ¶18)

  • Kodi ndi mfundo ziti zimene mwapeza pa kuwerenga Baibulo kwa mlungu uno?

3. Kuwerenga Baibulo

(4 min.) Miy 10:1-19 (th phunziro 10)

KUPHUNZITSA MWALUSO MU UTUMIKI

4. Ulendo Woyamba

(4 min.) KUNYUMBA NDI NYUMBA. Munthuyo wakuuzani kuti sakhulupirira kuti kuli Mulungu. (lmd phunziro 4 mfundo 3)

5. Ulendo Woyamba

(4 min.) KULALIKIRA MWAMWAYI. M’pempheni kuti muziphunzira naye Baibulo. (lmd phunziro 4 mfundo 4)

6. Ulendo Wobwereza

(4 min.) KULALIKIRA MWAMWAYI. Musonyezeni mmene angapezere nkhani yomwe ingamusangalatse pa jw.org. (lmd phunziro 9 mfundo 4)

MOYO WATHU WA CHIKHRISTU

Nyimbo Na. 111

7. Kodi Ndi Madalitso Ati Amene Amalemeretsa Atumiki a Mulungu?

(7 min.) Nkhani yokambirana.

Madalitso amene Yehova amapereka kwa atumiki ake m’masiku otsiriza ovuta ano, amatithandiza kuti tizipirira komanso tizikhala osangalala. (Sl 4:3; Miy 10:22) Werengani malemba ali m’munsimu, kenako funsani omvera mmene dalitso lililonse limawathandizira kukhala osangalala.

  • Yes 65:13

  • Lu 11:13

  • Yoh 13:35

Ena akwanitsa kuwonjezera utumiki wawo ndiponso kumasangalala kwambiri pa moyo wawo.

Zithunzi za muvidiyo yakuti “Achinyamata—Sankhani Njira Yomwe Ingakubweretsereni Mtendere.” 1. Harley. 2. Anjil. 3. Carlee.

Onerani VIDIYO yakuti Achinyamata—Sankhani Njira Yomwe Ingakubweretsereni Mtendere. Kenako funsani funso lotsatirali:

  • Kodi mwaphunzira chiyani kuchokera pa zimene zinachitikira Harley, Anjil ndi Carlee?

8. Lipoti la Dipatimenti Yoona za Mapulani Ndi Zomangamanga la 2025

(8 min.) Nkhani. Onerani VIDIYOYI.

9. Phunziro la Baibulo la Mpingo

(30 min.) bt mutu 25 ¶8-13, bokosi patsamba 201

Mawu Omaliza (3 min.) | Nyimbo Na. 115 ndi Pemphero

    Mabuku a Chichewa (1974-2025)
    Tulukani
    Lowani
    • Chichewa
    • Tumizirani Ena
    • Zimene Mumakonda
    • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
    • Zoyenera Kutsatira
    • Nkhani Yosunga Chinsinsi
    • Privacy Settings
    • JW.ORG
    • Lowani
    Tumizirani Ena