Magazini Yophunzira
MAY 2023
NKHANI ZOPHUNZIRA KUYAMBIRA: JULY 10–AUGUST 13, 2023
© 2023 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
Magaziniyi sitigulitsa. Timaipereka ngati njira imodzi yophunzitsira anthu Baibulo padziko lonse ndipo ndalama zoyendetsera ntchitoyi ndi zimene anthu amapereka mwa kufuna kwawo. Ngati mukufuna kupereka pitani pa donate.jw.org.
Malemba onse m’magaziniyi akuchokera mu Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika lolembedwa m’Chichewa chamakono, kupatulapo ngati tasonyeza Baibulo lina.
CHITHUNZI CHAPACHIKUTO:
Kungoyambira mu 1919 C.E., amuna, akazi ndi ana ambirimbiri akhala akutuluka mu Babulo Wamkulu ndipo ayamba kuyenda pa “Msewu wa Chiyero” (Onani nkhani yophunzira 22, ndime 8)