Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • wp25 No. 1 tsamba 1-2
  • Kodi Nkhondo Idzathetsedwa Bwanji?

Palibe Vidiyo.

Pepani vidiyoyi ikukanika kutsegula.

  • Kodi Nkhondo Idzathetsedwa Bwanji?
  • Nsanja ya Olonda Yolengeza Ufumu wa Yehova (Yogawira)—2025
Nsanja ya Olonda Yolengeza Ufumu wa Yehova (Yogawira)—2025
wp25 No. 1 tsamba 1-2
Mayi wagwira mwana wake atakhala pamulu wa zinthu zimene zagumulidwa mumzinda umene wawonongedwa ndi nkhondo. Iwo azunguliridwa ndi nyumba zowonongeka zokhazokha.

Kodi Nkhondo​—⁠Idzathetsedwa Bwanji?

© 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania

Magaziniyi sitigulitsa. Timaipereka ngati njira imodzi yophunzitsira anthu Baibulo padziko lonse ndipo ndalama zoyendetsera ntchitoyi ndi zimene anthu amapereka mwa kufuna kwawo. Ngati mukufuna kupereka ndalama, pitani pa donate.jw.org. Malemba onse m’magaziniyi akuchokera mu Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika, kupatulapo ngati tasonyeza Baibulo lina.

MAGAZINI ya Nsanja ya Olonda imalemekeza Yehova Mulungu, yemwe ndi Wolamulira wa chilengedwe chonse. Imalimbikitsa anthu ndi uthenga wabwino wakuti posachedwapa Ufumu wa Mulungu uchotsa zoipa zonse n’kusintha dziko lapansili kukhala paradaiso. Imalimbikitsanso anthu kukhulupirira Yesu Khristu yemwe anatifera kuti tidzapeze moyo wosatha ndipo panopo akulamulira monga Mfumu ya Ufumu wa Mulungu. Magaziniyi yakhala ikufalitsidwa kuyambira mu 1879 ndipo si yandale. Mfundo zake zimachokera m’Baibulo.

    Mabuku a Chichewa (1974-2025)
    Tulukani
    Lowani
    • Chichewa
    • Tumizirani Ena
    • Zimene Mumakonda
    • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
    • Zoyenera Kutsatira
    • Nkhani Yosunga Chinsinsi
    • Privacy Settings
    • JW.ORG
    • Lowani
    Tumizirani Ena