Mutu wa Buku Lino/Tsamba la Ofalitsa
Buku Lapachaka la Mboni za Yehova la 2017
Containing the Report for the Service Year of 2016
Bukuli ndi la ․․․․․
Photo Credits: Page 110: Georgian Bible: National Center of Manuscripts
Bukuli sitigulitsa. Timalipereka ngati njira imodzi yophunzitsira anthu Baibulo padziko lonse ndipo ndalama zoyendetsera ntchitoyi ndi zimene anthu amapereka mwakufuna kwawo.
Ngati mukufuna kupereka ndalama zothandizira ntchitoyi pitani pa www.pr2711.com.
Malemba onse m’bukuli akuchokera mu Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika, lolembedwa m’Chichewa chamakono, kupatulapo ngati tasonyeza Baibulo lina.
Losindikizidwa mu December 2016
© 2016
Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania