Zomwe Zili M’bukuli
Kalata Yochokera ku Bungwe Lolamulira 2
Zimene Zachitika M’chaka Chapitachi 6
Ntchito Yolalikira ndi Kuphunzitsa Padziko Lonse 11
Msonkhano watsopano wa Utumiki Komanso Moyo Wathu Wachikhristu 19
Mapulogalamu a pa JW Broadcasting ‘ndi othandiza komanso olimbikitsa kwambiri’ 24
Mwambo wotsegulira maofesi a nthambi 27
Malipoti apadera—Zochitika m’mayiko osiyanasiyana 39
Ntchito yolalikira ndi kuphunzitsa padziko lonse 46
Mfundo zachidule zokhudza dziko la Georgia 84
Anthu oyambirira kuphunzira choonadi 89
Misonkhano inawathandiza kukhala ndi chikhulupiriro cholimba 97
Ndinkafunitsitsa nditasintha zochita zanga 105
Ndinapempha Yehova kuti anditsogolere 106
“Zinthu zonse n’zotheka kwa Mulungu” 108
“Mulungu ndiye anakulitsa”—1 Akor. 3:6. 111
Anaphunzitsa ena kuti akhale akulu ndi atumiki othandiza 118
Mwamuna wanga sankafuna kusiya kuwerenga 128
Munali kuti nthawi yonseyi? 130
Ndinkaganiza kuti zinthu zikundiyendera 132
Chikondi chenicheni sichitha 134
Ndinaona ndi maso anga zimene Baibulo limanena 136
Anadalitsidwa ‘pa nthawi yabwino ndi pa nthawi yovuta.’—2 Tim. 4:2. 138
Sanasiye kutumikira Yehova ngakhale kuti ankaopsezedwa 145
“Ichi ndi cholowa cha atumiki a Yehova”—Yes. 54:17. 157
Anakumbukira Mlengi wawo Wamkulu 162
Anthu ambiri olankhula Chikadishi akuphunzira choonadi 169