YOBU
ZIMENE ZILI MʼBUKULI
1
Kukhulupirika kwa Yobu komanso chuma chake (1-5)
Satana anakaikira zolinga za Yobu (6-12)
Chuma cha Yobu chinawonongeka ndipo ana ake anafa (13-19)
Yobu sanaimbe Mulungu mlandu (20-22)
2
Satana anakaikira kachiwiri zolinga za Yobu (1-5)
Satana analoledwa kuti abweretse mavuto pa thupi la Yobu (6-8)
Mkazi wa Yobu ananena kuti: “Tukwanani Mulungu mufe!” (9, 10)
Anzake a Yobu atatu anabwera (11-13)
3
4
5
6
Yankho la Yobu (1-30)
Ananena kuti akuyenera kudandaula (2-6)
Anthu amene ankamutonthoza anali achinyengo (15-18)
“Munthu akamanena zoona, sizipweteka” (25)
7
8
9
Yankho la Yobu (1-35)
Munthu sangalimbane ndi Mulungu (2-4)
‘Mulungu amachita zinthu zosatheka kuzifufuza’ (10)
Palibe amene angatsutsane ndi Mulungu (32)
10
11
12
Yankho la Yobu (1-25)
“Si ine munthu wamba poyerekezera ndi inu” (3)
“Ine ndakhala chinthu choseketsa” (4)
‘Nzeru zili ndi Mulungu’ (13)
Mulungu ndi wapamwamba kuposa oweruza ndi mafumu (17, 18)
13
14
15
16
17
18
19
Yankho la Yobu (1-29)
Anakana kudzudzulidwa ndi anzake achinyengo (1-6)
Ananena kuti anzake apamtima amuthawa (13-19)
“Wondiwombola ali moyo” (25)
20
21
22
23
Yankho la Yobu (1-17)
Ankafuna kupititsa mlandu wake kwa Mulungu (1-7)
Ananena kuti Mulungu sakupezeka (8, 9)
“Ndapitiriza kuyenda mʼnjira yake ndipo sindinapatuke” (11)
24
25
26
Yankho la Yobu (1-14)
“Komatu ndiye wathandiza munthu wopanda mphamvu!” (1-4)
‘Mulungu anaika dziko lapansi mʼmalere’ (7)
‘Kambali kakangʼono chabe ka zochita za Mulungu’ (14)
27
28
29
30
31
32
33
34
35
36
37
38
39
40
41
42
Zimene Yobu anayankha Yehova (1-6)
Mulungu anadzudzula anzake atatu a Yobu (7-9)
Yehova anabwezeretsa mmene zinthu zinaliri pa moyo wa Yobu (10-17)