1 YOHANE
ZIMENE ZILI MʼBUKULI
1
2
Yesu, nsembe yophimba machimo (1, 2)
Kusunga malamulo ake (3-11)
Chifukwa cholembera kalatayi (12-14)
Musamakonde dziko (15-17)
Tichenjere ndi wokana Khristu (18-29)
3
Ndife ana a Mulungu (1-3)
Ana a Mulungu ndiponso ana a Mdyerekezi (4-12)
Muzikondana (13-18)
Mulungu ndi wamkulu kuposa mitima yathu (19-24)
4
5
Amene amakhulupirira Yesu amagonjetsa dziko (1-12)
Tizikhulupirira kuti pemphero ndi lamphamvu (13-17)
Tizisamala mʼdziko loipali (18-21)