Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • g01 12/8 tsamba 1-2
  • Zamkatimu

Palibe Vidiyo.

Pepani vidiyoyi ikukanika kutsegula.

  • Zamkatimu
  • Galamukani!—2001
  • Nkhani Yofanana
  • Nyamakazi Ndi Matenda Opundula Anthu
    Galamukani!—2001
  • Odwala Nyamakazi Asataye Mtima
    Galamukani!—2001
  • Kodi Akristu Ayenera Kugwiritsa Ntchito Njira Yotchedwa Fêng Shui?
    Galamukani!—2001
  • Kuwadziŵa bwino Matenda a Nyamakazi
    Galamukani!—2001
Onani Zambiri
Galamukani!—2001
g01 12/8 tsamba 1-2

Zamkatimu

December 8, 2001

Odwala Nyamakazi Asataye Mtima

Matenda a nyamakazi amagwira anthu ochuluka zedi, akulu ndi ana omwe. Kodi n’chiyani chimene chimayambitsa matenda opundulaŵa? Kodi n’chifukwa chiyani odwala angayembekezere kudzachira m’tsogolo?

3 Nyamakazi Ndi Matenda Opundula Anthu

5 Kuwadziŵa bwino Matenda a Nyamakazi

9 Odwala Nyamakazi Asataye Mtima

13 Nkhani ya Dzina la Mulungu Inabutsa Mkangano

19 Anthu Akupulula Zinthu Zachilengedwe

20 Zachilengedwe Zimadalirana M’njira Zovuta Kuzimvetsa

26 Kodi M’tsogolomu Zinthu Zidzakhala Bwanji?

28 N’chifukwa Chiyani Muyenera Kuŵerengera Ana Anu Mokweza Mawu?

31 Zisonyezero za Voliyumu 82 ya Galamukani!

32 Kodi Angandiyankhe Ndani?

Kodi Akristu Ayenera Kugwiritsa Ntchito Njira Yotchedwa Fêng Shui? 14

Njira ya fêng shui yomwe n’njochokera ku mayiko aamwenye ikutchuka kwambiri kumayiko aazungu. Kodi Akristu ayenera kuiona bwanji?

Kodi Anthu Amtima Wapachala Ndingachite Nawo Bwanji? 16

Onani zimene mungachite kuti mupeŵe kukwiyitsa anthu.

    Mabuku a Chichewa (1974-2025)
    Tulukani
    Lowani
    • Chichewa
    • Tumizirani Ena
    • Zimene Mumakonda
    • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
    • Zoyenera Kutsatira
    • Nkhani Yosunga Chinsinsi
    • Privacy Settings
    • JW.ORG
    • Lowani
    Tumizirani Ena