Zamkatimu
March 8, 2002
Kodi Tidakatani Padakapanda Aphunzitsi?
N’zotheka kuti pamagulu onse a anthu amene amagwira ntchito padziko lonse, aphunzitsi ndiwo ochuluka kwambiri. Tonsefe tinafika pamene tilipa chifukwa cha khama lawo potiphunzitsa. Koma kodi n’zinthu zotani zimene zimavuta ndiponso kusangalatsa pophunzitsa?
3 N’Chifukwa Chiyani Timafunikira Aphunzitsi?
12 Uphunzitsi Uli M’pokomera Pake
20 Achinyamata Akufunsa Kuti . . .
Kodi Zingakhale Bwanji Ngati Nditakumana ndi Winawake wa Kusukulu Kwathu?
23 Zochititsa Kuti Kuntchito Kukhale Koopsa
24 Kukhala Otetezeka Kumalo Anu Antchito
27 Malingaliro Oyenera a Ntchito
32 Mmene Anapezera Mphoto Yoyamba
Amasai—Anthu Odabwitsa Ndiponso Ochititsa Kaso 16
Moyo wa anthu okongola ameneŵa amene amakhala m’chigawo cha Kummaŵa kwa Africa muchita nawo chidwi kwambiri.
[Mawu a Chithunzi patsamba 3]
COVER: UNITED NATIONS/RAY WITLIN