Zamkatimu
January 8, 2003
Khoti Lalikulu ku America Ligamula za Ufulu Woyankhula
Oweruza 8 pa oweruza 9 a Khoti Lalikulu ku United States anavotera zakuti anthu azikhala ndi ufulu wouza ena nkhani zinazake popanda kukatenga kaye chilolezo kuboma. Kodi ndi mfundo zotani zimene zinachititsa oweruzawo kuvota motero?
4 Khoti Lalikulu Livomera Kumva Mlanduwu
6 Choyamba Khoti Lalikulu Limva Mlanduwu
9 Khoti Lalikulu Ligamula Kuti Pakhale Ufulu Woyankhula
12 Mmene Mungatetezere Pathupi Panu
22 Galimoto, Zamakedzana ndi Zamakono
28 Kuvutikira Chikhulupiriro ku Slovakia
Ndinasiya Khalidwe Lokakala Mtima 18
Onani mmene Baibulo linasinthira munthu wina amene ankafuna kupha anthu pofuna kubwezera.
[Mawu a Chithunzi patsamba 2]
COVER and above: Photo by Josh Mathes, Collection of the Supreme Court of the United States
Gerken/Naturfoto-Online.de