Zamkatimu
July 8, 2004
Kuthana ndi Mavuto Amene Amakhalapo Achinyamata Akamakula
Wachinyamata akamakula akuti amakhala ngati akuyenda pa kachingwe koonda popanda chinachake pansipa choti chimuwakhe akagwa. Kodi angatani kuti zinthu zimuyendere bwino?
3 Zosangalatsa ndi Zovuta Zimene Zimakhalapo Achinyamata Akamakula
4 ‘Kodi Chikuchitika N’chiyani M’thupi Mwangamu?’
10 Kuyeza Dziko Lapansi ndi Ndodo
11 Kodi Kukhulupirira Mulungu N’kusemphana ndi Sayansi?
13 Zifukwa Zimene Asayansi Ena Amakhulupirira Mulungu
18 Kodi Mayankho Mungawapeze Kuti?
24 Lavenda Mphatso Imene Imasangalatsa Lilime, Maso ndi Mphuno Zathu
32 Mayi Wanzeru
Kodi Ndingatani Kuti Chibwenzi Changa Chisiye Kundizunza? 21
Kodi mungatani ngati muli pachibwenzi ndi munthu amene amakulankhulani mawu opweteka, ngakhale kukumenyani kumene?
Moŵa—Mbiri ya Chakumwa cha Maonekedwe a Golide 28
Anthu akhala akufulula moŵa kwa zaka zambiri. Tamvani mbiri yake yochititsa chidwi.