Zamkatimu
October 2011
Galamukani! Yapadera
Kodi Mungalere Bwanji Ana Anu Kuti Akule Bwino?
KHANDA TSAMBA 4 MPAKA 9
4 Ubongo wa Mwana Umaphunzira Zinthu Mogometsa Kwambiri
MWANA WAMNG’ONO TSAMBA 10 MPAKA 15
10 Kulera Ana Azaka Zapakati pa 5 ndi 12
WACHINYAMATA TSAMBA 16 MPAKA 23
16 Kuthandiza Achinyamata Kuti Akule Bwino
32 Mabuku Oti Ana Aziphunzira Pamene Akukula