Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • g05 5/8 tsamba 1-2
  • Zamkatimu

Palibe Vidiyo.

Pepani vidiyoyi ikukanika kutsegula.

  • Zamkatimu
  • Galamukani!—2005
  • Nkhani Yofanana
  • Kodi Ziri Nkanthu Kuti Ndiakanema Otani Amene Ndimawonerera?
    Galamukani!—1990
  • Kodi Tizigwiritsa Ntchito Zithunzi Popemphera?
    Galamukani!—2005
  • Nchiyani Chimene Chiri Chowopsya Motero Ponena Za Makanema Owopsya?
    Galamukani!—1988
  • Mmene Mafano Azithunzi Zachipembedzo Anayambira Kalelo
    Nsanja ya Olonda—2002
Onani Zambiri
Galamukani!—2005
g05 5/8 tsamba 1-2

Zamkatimu

May 8, 2005

Kodi Mafilimu Akukhala Otani Masiku Ano?

Anthu ambiri akuda nkhawa chifukwa cha kuchuluka kwa kugonana ndi chiwawa m’mafilimu. Ngati mukufuna kuti anthu a m’banja mwanu aonere mafilimu, kodi mungasankhe bwanji mwanzeru mafilimuwo?

3 Kodi Akuonetsa Mafilimu Ati Chilimwe Chino?

4 Kuchoka pa Nkhani Kufika pa Filimu

8 Kodi Inuyo Muonera Mafilimu Ati?

15 Kodi Yesu Kristu Ndi Ndani?

17 Kodi “Mulungu Woona Yekha” Ndi Ndani?

20 Imene Imatchedwa “Milungu”

10 Zimene “Mulungu Woona Yekha” Walonjeza

27 Ndinatha Kutumikira Mulungu Ngakhale Zinali Zovuta

32 Achinyamata Akufunafuna Mayankho

Kodi Tizigwiritsa Ntchito Zithunzi Popemphera? 13

Kugwiritsa ntchito zithunzi zachipembedzo popemphera ndi mbali yofunika kwambiri m’zipembedzo zochuluka. Kodi Baibulo limati chiyani pa nkhani imeneyi?

“Kodi Ndipeze Chibwenzi pa Intaneti?” 24

Amuna ndi akazi ambiri okwatirana amadziwana koyamba pa Intaneti. Kodi n’chifukwa chiyani anthu ambiri amakonda kupeza zibwenzi pa Intaneti? Kodi kuopsa kopeza chibwenzi pa Intaneti n’kotani?

[Mawu a Chithunzi patsamba 2]

Boris Subacic/AFP/Getty Images

    Mabuku a Chichewa (1974-2025)
    Tulukani
    Lowani
    • Chichewa
    • Tumizirani Ena
    • Zimene Mumakonda
    • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
    • Zoyenera Kutsatira
    • Nkhani Yosunga Chinsinsi
    • Privacy Settings
    • JW.ORG
    • Lowani
    Tumizirani Ena