Zamkatimu
December 2010
Kodi Khirisimasi Inayamba Bwanji?
Werengani nkhanizi kuti muone mmene kudziwa chiyambi cha Khirisimasi kwathandizira mabanja ena.
3 N’chifukwa Chiyani Anthu Ambiri Akukondwerera Khirisimasi Masiku Ano?
5 Kodi Khirisimasi Inayamba Bwanji?
12 Mulungu Wanditonthoza M’mayesero Anga Onse
20 Tiyembekezere Zivomezi Zinanso Zikuluzikulu
22 Zimene Achinyamata Amadzifunsa
Kodi Ndingafotokoze Bwanji Zimene Baibulo Limanena pa Nkhani Yogonana Amuna Kapena Akazi Okhaokha?
30 Mlozera Nkhani wa Magazini a Galamukani! a 2010
32 Ankaphunzirira Limodzi ndi Ana Ake
Bwanji Mulungu Osangomuwononga Mdyerekezi? 10
Baibulo limatitsimikizira kuti Mulungu adzawononga Satana pa nthawi yoyenerera. Werengani nkhaniyi kuti mudziwe chifukwa chake sanamuwonongebe mpaka pano.
Chivomezi cha ku Haiti Chinapereka Mpata Wosonyeza Chikhulupiriro ndi Chikondi 14
Chivomezi chimene chinachitika ku Haiti mu January 2010 chinagwetsa nyumba zambiri komanso kupha anthu oposa 200,000. Werengani nkhaniyi kuti mumve mmene anthu anadziperekera kuti athandize anthu okhudzidwa ndi chivomezichi komanso mmene anapulumutsira anthu ndi kuwapatsa chiyembekezo.