Zamkatimu
August 2014
© 2014 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
NKHANI YA PACHIKUTO
Kodi Mungatani Kuti Mugwirizanenso Ngati Mwayambana?
TSAMBA 3 MPAKA 6
MUNGAWERENGENSO NKHANI ZOTSATIRAZI PA WEBUSAITI YATHU YA
ACHINYAMATA
Mungapeze mayankho ochokera m’Baibulo a mafunso ambiri amene mungakhale nawo. Nkhani zake ndi monga:
• “Kodi Ndingatani Kuti Ndikambirane ndi Makolo Anga pa Nkhani ya Malamulo Amene Anandiikira?”
• “Kodi Ndithetse Chibwenzichi?”
Mungathenso kuonera vidiyo yachingelezi yakuti, What Your Peers Say—Healthy Lifestyles pa webusaiti yathu ya www.jw.org/en.
(Fufuzani pa mawu akuti ZIMENE BAIBULO LIMAPHUNZITSA > ACHINYAMATA)
ANA
Werengani nkhani zomwe zafotokozedwa pogwiritsa ntchito zithunzi. Gwiritsani ntchito nkhanizi kuthandiza ana anu kudziwa zambiri za anthu otchulidwa m’Baibulo komanso kuwathandiza kuti akhale ndi makhalidwe abwino.
(Fufuzani pa mawu akuti ZIMENE BAIBULO LIMAPHUNZITSA > ANA)