Zamkatimu
November 2014
© 2014 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
NKHANI YA PACHIKUTO
Kodi Mungatani Kuti Muzisangalala?
TSAMBA 4 MPAKA 7
8 Ngalande za Madzi za ku Roma Ankazimanga Mwaukadaulo
12 Yehova Anandithandiza pa Nthawi Yomwe Ndinkafunikiradi Kuthandizidwa
16 Nyumba Yomwe Imakumbutsa Anthu za Bomba Loopsa
MUNGAPEZE ZAMBIRI PA WEBUSAITI YATHU YA
ACHINYAMATA
Mungapeze mayankho ochokera m’Baibulo a mafunso ambiri amene achinyamata amadzifunsa. Nkhani zake ndi monga:
• “Kodi Ndingatani Kuti Ndisamangokhala Wokhumudwa?”
• “N’chifukwa Chiyani Ndikufunika Kumathandiza Ena?”
Mungathenso kuonera vidiyo yachingelezi yakuti, “What Your Peers Say—Money” pa webusaiti yathu ya www.jw.org/en
(Fufuzani pa mawu akuti ZIMENE BAIBULO LIMAPHUNZITSA > ACHINYAMATA)
ANA
Werengani nkhani zomwe zafotokozedwa pogwiritsa ntchito zithunzi. Gwiritsani ntchito nkhanizi kuthandiza ana anu kudziwa zambiri za anthu otchulidwa m’Baibulo komanso kuwathandiza kuti akhale ndi makhalidwe abwino.
(Fufuzani pa mawu akuti ZIMENE BAIBULO LIMAPHUNZITSA > ANA)