Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • sn nyimbo 9
  • Tamandani Yehova, Mulungu Wathu!

Palibe Vidiyo.

Pepani vidiyoyi ikukanika kutsegula.

  • Tamandani Yehova, Mulungu Wathu!
  • Imbirani Yehova
  • Nkhani Yofanana
  • Tamandani Yehova Mulungu Wathu
    Imbirani Yehova Mosangalala
  • Tamandani Mwana Woyamba Kubadwa wa Yehova
    Imbirani Yehova Mosangalala
  • Imbani Chitamando cha Yehova Molimbika!
    Imbirani Yehova Zitamando
  • Yehova Amafunikira Chitamando Chosatha
    Nsanja ya Olonda​—1990
Onani Zambiri
Imbirani Yehova
sn nyimbo 9

Nyimbo 9

Tamandani Yehova, Mulungu Wathu!

Losindikizidwa

(Salmo 145:12)

1. Tamanda! Yehova M’lungu!

Dzina lakelo lengeza!

Chenjeza! Adziwe kuti

Tsiku lake layandikira.

Mulungu walengeza za ulamuliro

Wa Mwana wake.

Kauzeni anthu uthengawu,

Ndi madalitso akenso!

(KOLASI)

Tamanda! Yehova M’lungu!

Lengeza kuti ndi wamkulu!

2. Tamanda! Mokweza mawu!

Mosangalala imbani!

Ndi mtima, woyamikira

Tilengeze ulemerero.

Mulungu ndi wamkulu kwambiri

Koma ndi wodzichepetsa,

Wokoma mtima ndi wachikondi,

Adzamva pemphero lathu.

(KOLASI)

Tamanda! Yehova M’lungu!

Lengeza kuti ndi wamkulu!

(Onaninso Sal. 89:27; 105:1; Yer. 33:11.)

    Mabuku a Chichewa (1974-2025)
    Tulukani
    Lowani
    • Chichewa
    • Tumizirani Ena
    • Zimene Mumakonda
    • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
    • Zoyenera Kutsatira
    • Nkhani Yosunga Chinsinsi
    • Privacy Settings
    • JW.ORG
    • Lowani
    Tumizirani Ena